Email a copy of 'Malawi nutritionist says breast milk pumping should be encouraged' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

3 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Chakanda Kawonga
Chakanda Kawonga
6 years ago

Nkhani yabwino kwambiri imeneyi bcoz its an alternative kwa amene palivuto kuti ayamwise mwakathithi mwana wawo mwina pa zifukwa ngati kudwala kapena ku ntchito komwe mwina pa zifukwa zina akuona kuti sangakwanise kukayamwisila mwanayo ku ntchitoko. Kwa amene sangakwanise kupeza zipangizo ngati awonesa pa mwambozo i hope anenaso kuti kuti mutha kugwirisa ntchito manja…

nsanai kugwe
nsanai kugwe
6 years ago

izi musaziyambitse mulibe zipangizo zothandizila anthuakadwala nazo izi. nza anthu olemera izi.
abwana siyani kulimbikila ntunda opanda madzi. dziko lathuli lili kutali zedi to implement the issue. inu munayamwa mpaka kukula olo amanu kufinya mkaka , anthu amafinya nkaka zikavuta pa dzana lija. nde muzipeleka zipangizo zake??? komaso anthu pofunila kuchuka>??????? bwanji osangolimbikitsa njila zomwe zilipozi. kkkkkkkkkkkkkkk

Catherine Mkangama
Catherine Mkangama
6 years ago
Reply to  nsanai kugwe

The comments above are good…..the most important thing is to agree that Breast milk is the best and most important food for the child for it does not only save life but it also improves the quality of life. Mwana sadwaladwala chifukwa mu mkaka wa mmawere muli chitetezo chomwe chimathandiza mwanayu, muli zakudya zonse zofunikira kuphatikizapo madzi kuti mwana akule bwino. Choncho kumpatsa mwana mkakawu okhaokha mpaka miyezi 6 from birth (180 days) ndi chinthu chofunika kwambiri. Akakwana miyezi 6 ayamwebe kwinaku mukumpatsa zakudya zina zoyenera za magulu 6 zimanenedwa zija.. Koma amayi ena amakhala kuti ali pa ntchito olo… Read more »

Read previous post:
 Malawi entrepreneurs urge Mutharika to assent to Procurement bill

Local entrepreneurs have added their weight to the amended Procurement and Asset Disposal Bill, urging President Arthur Peter Mutharika to...

Close