Email a copy of 'Malawi Police arrest Admarc guard over killing' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
The Prophet
7 years ago

Mesa munkanena kuti Nzimayi ndiwoyipa dizo mwaziona koma mukungoyang’ana akanakhala nthawi ya nzimayi mukanati ndiosaphunzira nkuona njala yamukanika nanga ophunzirawo zikuwakanika bwanji pano. Malawi khala odekha ndipo siuyamika siunati ukukolola zimene unadzala. How I wish 2019 azawinenso yemweyu chifukwa siuyamika kwamulungu. Kumbuka atakuchotsa ku Egiputo kuputa nawe ku kenani unamunyoza kuti wandichitseranji siiizo umafuna zija nanga ukulira chani lero. Kumbuka phunzira yamika ndinso khala ndi nzeru. Ngati nkotheka uziyamika mulungu akakuchotsa mmavuto.

chikopa
chikopa
8 years ago

An accident happened. How can the police say he should have locked the gun when people trampled on him? I think most commentators here only have a sheer hatred of Peter and are mbwenu-mbwenu. The Nsanje people were not die out of hunger but rather impatient. Can you please remember they killed seven people by burning in a single day? They are hard-hearted. Kukonda kulenga ng’ona and so many bad things. Look at people like Mbuya from Chikwawa and rest of them. Their intention was not to pay for the maize. So please most of the dickheads who have commented… Read more »

Ayaya kumudzi
Ayaya kumudzi
8 years ago

Please release him on bail.This is an accident there was no motive whatsoever to kill. The case of negligence does not arise here.

Nabetha
Nabetha
8 years ago

Musiyeni munthu wa anthu. umboni muli nawo kuti sichinali cholinga chake kutero koma anthu ndiamene amamusokoneza, kumulepheletsa kuti asagwire ntchito yake mwadongosolo.

Kwa banja la munzathu watisiyayo tikungoti pepani ndithu. Mulungu yekha akutonthozeni.

Mob
Mob
8 years ago

Peter? Do you see now that a person has died in Nsanje for food?

Bima Matheza
Bima Matheza
8 years ago

APM his death happened due to shortage maize. pLZ Listen to wise pple 4 advice

Zoona
Zoona
8 years ago

No body has died because of hunger in Malawi. Now it makes sense. Sichoncho Kasaira ndi Peter Mutharika?

kk
kk
8 years ago

That’s what i know kuti njala ikakula msinkhu imatha kupangisa anthu osauka kumaoneka ngati nyama za ku tchire mmaso mwa anthu olemera,tell me what is the use of the gun pamalo pamene anthu akufuna chakudya?
Ndipo nchifukwa chiani Boma likunnamabe mpaka lero kuti chakudya lili nacho chokwanila?
Ndipo likumakanabe kuti palibe anthu omwe afapo ndinjala, kodi munthuyu si njara yomwe yamuphetsa?Malawi! Malawi! Malawi! Kodi tiyelekeze kuti mwina ndivuto la utsogoleri pomatha zaka zotsalazi zitithera bwaaa! nanga tiyerekeze mwa umbuli muja tichitenso mwina ndikulola kuti utsogoleri upitilile, anthu akahalapobe?
kaya ine ndangofusako sindidatchule munthu, kapena dzina la munthu, nangodandaula ine!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

Mbodzole
Mbodzole
8 years ago

Barely after a few days some dunderhead refused to accept the reality of hunger related deaths in the country, here a life has been lost as a result of a struggle for maize at an Admarc depot… chickens coming to roost

Read previous post:
Irate villagers seal off DC’s office in Salima

Irate villagers in Salima have sealed off the district commissioner’s office and erected a road block preventing him from going...

Close