Email a copy of 'Malawi Police arrest man for stabbing woman over K750 000 debt' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

12 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Buba
Buba
6 years ago

kodi zinthuzi ndizakubanja eti? sister wa a guy wa, Sarah, anamuombanso mwamuna wina wake dollar, akuti amakalipira fees yaku Health Science, kenako ndikumathawa guy ikamufunsa.

calculus
calculus
6 years ago

eeeeeeeish koma anthu ena ake nkhanzaaa……… end time events

Amfana
Amfana
6 years ago

Chemjambe, zikuwoneka kutitu mkaziyu ndi yemwe anapereka Dollar kwa man wa. Nde amakumbutsa dollar zache mayiyu pafupipafupi Phiriwa powona kuti dollar yashuzya patauni, anamunamiza mkaziyu kuti akumufuna kuti abweze dollar. Koma anamulakwila kwambiri nanga zache zomwe pilizi???

Matako
Matako
6 years ago

Okay akulu! Yankhulani mokutha mawa zamanyi zanuzo!

mvvuuuu
mvvuuuu
6 years ago

shouldnt he also answer charges of attempted murder?

Chemjambe
Chemjambe
6 years ago

Ankolo kukongoza ndalama mkazi ndi chimodzimodzi kukataya mu nyanja, mkazi sabwenza ngongole boss. pepani mwaluza kangachepe kanu apa

Tracy
Tracy
6 years ago
Reply to  Chemjambe

Its the man who borrowed money from Sally.

Ineyo
Ineyo
6 years ago
Reply to  Chemjambe

Chemjambe, ankolo anuwa ndi omwe anakongola ndalama kwa mkazi osati mkazi kukongola kwa ankolo anuwo. Abaya mkazi chifukwa chokanika kubweza ngongole kwa mkaziyo

FAN
FAN
6 years ago
Reply to  Chemjambe

Sukulu munadumphira eti………. The man is the one obweleka ndalama ka from the lady…..

Anyway, did he really stabbed her or merely threatened her……. Because there’s no way a multiple stab wound (s) patient can be treated as an outpatient

Mariko Mariko
Mariko Mariko
6 years ago
Reply to  Chemjambe

Abambo man wa ngopusa its him actually who borrowed from the woman ndiye when the woman was asking for her man iwowo basi he decided to silence the woman.

Chilombo
Chilombo
6 years ago

Kodi ndiwaku 18 eti. The power of drinking manyi, amuzunguza ubongo mpaka kubayanzake

Rashied
6 years ago
Reply to  Chilombo

That’s bed fear God men

Read previous post:
First Lady urges Malawi youth to take lead in national development

The First Lady Gertrude Mutharika has called on youths in the country to jealously guard the peace and tranquility that...

Close