Email a copy of 'Malawi Police launch manhunt after armed robbery at Mangochi DC’s office' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi Police launch manhunt after armed robbery at Mangochi DC’s office' to a friend
The progress of the construction of the K504 million Karonga Stadium at Baka in the district – a project under...
That’s DPP gvnt! No wonder!
Now looking at the situation, what can Malawians do when they catch these animals if the police are failing their work? Mob justice is the only viable option. Eliminating 12 thieves from the face of the earth and Malawi in particular would be a great achievement as far as security is concerned. Those who are involved in robberies and theft have forfeited their capital (life) once caught by the community.
Akuba ndi apolisiwo nanga neba kukhala polisi mbavazo osadzigwira..Zodabwitsa zedi
Ku Mangochi kukuchitika zinthu zambiri zosakhala bwino. Khansala wina ‘adamubera’ MK2.8Million ku Resthouse! Kodi chisimo chosunga ndalama mu ofesi chikupitilirabe? Kalipo kalipo ndithu!
this is a shoot to kill situation…. no mercy
Kusunga ma certificates ku office? Bwana DC munaganiza bwanji pamenepa? Ndiye akubawa anaomba mfuti pofuna kuophyeza anthu? Apolisi akumangochi amatani nthawi imeneyo popeza office ya DC sili kutali ndi police? Apolisiwa sanamve kulila kwa mfuti?
bwana DC amakonzekela head cont,any way koma wy ma certificates nzanu anavutika kusala tulo ndikuwelenga inu mukatani nazo ngati pali dzina lanu plz fynd a way kawabwezeleni bwanawo
Police yathu ndiyodzidzira akanakhala oba nkhuku atamgwira kale.. Bola apange hire a g4s igwira
Can I conclude that those who escaped from Mangochi prison are behind this robbery. Kill one kill them all when found because these beasts are a nuisance to Malawi.
DC akuziwapo kathu Apolice pena pake kumamvetsesa nkhani pali zikuchiti timva kumapeto awake