Email a copy of 'Malawi Police ‘ready’ for demo: Mbewe, Usi blame CSOs' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

168 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
chidwi
9 years ago

Mtambo, why cant you start preparing for moyo wanu wakumwamba popeza kachilombo kanakuzwitani kale. Osathokoza Mulungu kuti wakupatsani mwayi woti mulape, mukamauza azungu kuti aleke kuthandiza boma la Malawiri ma ARV mukawatenga kuti inuyo, ku Nyika? Mungogeya mwano muli mumahotela akuno ku Malawi kwanu tchile lili thooooo ndichifukwa mukukanilira kwa anzanu kwanu mumasowa kopangilako misonkhano. Batimangilani nyumbazi kwathu kuno mudzazisiya ngati momwe mudatisiyitsila ife nyumba zathu ku Mzuzu achawafe a UDF

chatty man
chatty man
9 years ago

Onse akutukwana anadya nawo

Mbwiyace
Mbwiyace
9 years ago

Mbewe and Usii are right. I think Mbuya ananena bwino kuti maburutu achuluka ku Malawi.

anjomba
anjomba
9 years ago

zoopsyezana tatopa nazo.dziko silanu nokha a nac athu akuvutika kusowa chithandizo muku gawa ndalama kumphwando la presdnt icho nde chinyengo.ngati simuntha ntchito surendani agwile ena not imbombo zyo mwanda izya kumatanga ha.

Chilungamo Chimawawa
Chilungamo Chimawawa
9 years ago

A Manganya asanduka mbola masiku ano. Amayitenga ADRA ngati bungwe la mbuyache . he is into politics now buying favours from DPP

Blessings khonje
9 years ago

KKKKK akuluakulu to run agovernment is not easy dont accuse others but just polish ones mistake.Mr Manganza musatiwonongere ka program kathu talk zinazi outside.

Atonga
Atonga
9 years ago

No one can demostrate without proper reason.weather rubish people can say no to demo or yes.demostrations are justifyed.

Maliseni
Maliseni
9 years ago

WHY DEMONSTRATING AGAINST MK 5 MILLION AND WHEN WE LOST BILLIONS TO LATE BINGU AND JB ???????????????????? CSOs THINK USING BRAINS PLEASE.

Mbwinda
Mbwinda
9 years ago
Reply to  Maliseni

Plse dont deliberately choose to contract urself. its bad people didnt demonstrate then for the cashgate past mistake. shud they still remain irresponsible? well done to be demonstrators bcoz u ve learnt from mistake. kupha
nyani nkusayang’ana nkhope.

Mbwinda
Mbwinda
9 years ago
Reply to  Maliseni

Plse dont deliberately choose to contradict urself. its bad people didnt demonstrate then for the cashgate past mistake. shud they still remain irresponsible? well done to be demonstrators bcoz u ve learnt from mistake. kupha
nyani nkusayang’ana nkhope.

Munthu odzikonda mtumbuka
Munthu odzikonda mtumbuka
9 years ago

Demo ya atumbuka iyi yazamkutu as usual!

Alungwana
Alungwana
9 years ago

Manganya has even turned Tikuferanji into politics, should we inform ADRA?

Read previous post:
Paladin’s Walker must go, Kyungu tells Malawi govt

Paramount Chief Kyungu has asked Malawi government  to give country director of Australian-registered Paladin Africa Limited, Greg Walker, removal directions...

Close