Email a copy of 'Malawi ‘spy chief’ guilty over K34mil fraud: Court orders Thodi to repay MP Navicha' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi ‘spy chief’ guilty over K34mil fraud: Court orders Thodi to repay MP Navicha' to a friend
Former chief executive officer for the State produce trader, Agricultural Development and Marketing Corporation (Admarc), Foster Mulumbe on Tuesday told the...
Asaaaaaa. A Thodi ndalama mmanyengera a zimai a eni ake zija ndizakuba??? A Mary aja amafera ndalama as eni ake????? Daaaaamn
Asatinamizepo awa. Bvuto lawo ndi lakuti akhala akunyengana kwa nthawi yaitali! Kaya anthu amakonda zokodzerana ndikutulutsa mkaka chifukwa chiani?
Friendly fire. Okhaokha kumenyana.
The conviction alone is an enough one way ticket out of civil service… For morality and integrity sake, we cannot have a country’s national intelligence chief being a fraud convict; this is moral turpitude of the highest order.
These are the trusted pepo from DPP!! hahahahahah
reliable people of HE……..
Mbava… Tsopano munthu ngati uyu nkumakhala pa helm ya chitetezo cha dziko a Chasowa akhala angati? Eish!!!Koma boma ili. Ambuye tikhululukureni….A Navicha koma Chitetezo chanu ndi chokwanir”? Tisamve zoti mwasowatu. Munthu woophyatu uyu.
a thodi mumafuna kumuomba mzimayi bwezani ndalamazo bwanji ndalama sizimakukwanani mwadya zambili ku immigration pano mwati mumufwambe navicha shaaa mwayaluka
Mr president
Is this type of people you give responsibility? Just like Dr ntaba.
Please do not ask me!!! Ask the court.
Have a good day sir
These are the Government officials that the DPP Government appoints. He cannot be fired I bet.