Email a copy of 'Malawi squad leaves for Cosafa: Gaba, Jose and ‘Baggio’ not included' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

35 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Hardson
8 years ago

Komanso timangodandaula team silibwino ifenso ma supporter tilibe luso olo mpang’ono pomwe timaonetsa usapota team ikachinya ngati Jeffrey Msampha kapena Steve Banda pa commentery; ifeyo tinayenera kusapota from word go to the word stop osati kungochinyidwa ndiye ngati kwagwa maliro stadium yonse ziii. Aaaaaa ku Malawi palibe chilipo!!!!! Taganizani commentator (mMalawi) kugulitsa game ya dziko lake lomwe kkkkkkkkk hehedeee ulu.

Hardson
8 years ago

The problem is with our players. Can you imagine Kamwendo denied a call up saying he is paving way for new blood; is that ok? Walemera…..

walker
walker
8 years ago

ine ndi m,modzi mwa anthu oyenda ndi mi pini kubwera ku stadium kuzakugendani ndi anthu ako ameneoo musadzayende mu streat ndizaku bayani ndi mpeni

Mc Duff Phiri
Mc Duff Phiri
8 years ago

Zomakalowetsa Ma Right Winger Okhaokha Five Kuti Asewere Pa Midfield Ayi Zichepe…We Expect Much Frm U Guyz

timi
8 years ago

Welcome to xenophobia………

Kanyama Chima
Kanyama Chima
8 years ago

I hope mwatenga team not just a bunch of players.

collin jr
8 years ago

you just wasting ur tym and money going to RSA coz u can’t succeed

mbindinga
mbindinga
8 years ago

young,simunamutenge Tizgo ali pa peak ku BB,mukamutenga pano coz ali ku silver?Mc donald ndi goalkeepr yemwe wachinyitsa zigoli zambiri,inu kukatenga yemweyo,defender wa civo emwe akupita ku B4ward sanamenyeko compititive game since last season….kaya ife athu ndi maso

mphatso
mphatso
8 years ago

this is just a trial and error team.they never win anything

mbani
8 years ago

Walter how on earth?

Read previous post:
I remain UDF leader – Atupele Muluzi

Minister of Home Affairs and Internal Affairs Security, Atupele Muluzi has said he remains the president of United Democratic Front...

Close