Email a copy of 'Malawi tax body seizes documents from Chakwantha law firm: MCP lawmaker accused of tax evasion' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi tax body seizes documents from Chakwantha law firm: MCP lawmaker accused of tax evasion' to a friend
Malawi Telecommunications Limited (MTL) has reaffirmed its commitment to improved service delivery to its customers. The company made the assurance...
A lawyer zikuonekatu kuti boma mumafuna kulanda lija tsono latsala pang’ono kukunjatani. Kumenekutu ndi kuba. Wina wake adanena kuti wakuba ndi amene wagwidwa. Chimodzimodzi wachita chigololo ndi uyo wagwidwa mnyumba mwa anatsibekowo. Amwenye akumangidwatui ndi nkhani ngati izi, tsono inu ndiye musamangidwe? Mukavala sanza please musamadumphe moto mungadzaotche nyung’unyu.
Iwe # 16 ndi amzako ena mwabadwa liti inu mukamati DPP ndima criminal? Ufunse agogo ako or agogo anu nonse akuwuzeni za MCP momwe anawaphera a Gadama Matenje Ciwanga ndi Sangala komanso Madinga Cipembere Kwapatila Mhango Chisinza Nyirenda Mwafulirwa Manda Singini Cikhungwa Mbale ndi ena ambiri monganso SOLOBALA. Ngakhale zitavuta motani sizizathekanso kuti MCP mkuzalamulira muno mmalawi. Anacita nkhanza zowopsya monga makhadi nyakula misonkho fees ku primary kuponya anthu paziwe kuti adibwe ndi ng’ona kulanda anthu malo nyumba mafarm kulanda anthu mbuzi ng’ombe nkhuku mazira mkazi wakonso ndizina zotero.
Ma lawyer ose ndi chimodzimodzi, chavuta apa nchoti uyu wawinitsa MCP mlandu KU coirt , after enawo anapanga masamu osokoneza MCP momemeza ena my MCP kuti aukire nkutengera MCP kiu court kutiipangitse convention so that kiu convention akachotse achina chakwera pa mpando…kkkk nkhanga zawona.
Kodi za M & M global law consultants zili pati paja munalandaso ma documents becoz tax evasion.
Most law firms evade tax. If this exercise was done to all legal firms, the country would surprised how much government is losing each month in undeducted or unremitted tax returns.
For every opposition tax evader or criminal, there are ten dpp gurus tax evaders or criminals. So mra if you are serious about this thing then target dpp gurus also. And please don’t tell us that you know them dpp thieves. Witch hunting mcp officials, especially parliamentarians will take you no where you dpp mra puppets. Because dpp is so full of criminals, you have been ordered to balance the imbalance of criminality by fabricating criminality issues on the opposition. Dpp is so heavily tarnished with thieving and thuggish behaviors that it now wants the opposition also to be tarnished… Read more »
Blessed Hope Isulu letter to the public on youth is good news
Boma ndi Boma basi. Silimaluza. Bingu anatero.
Kaya zanu izo, munaziputa dala.
Obviously, politicians like everybody else are prone to criminal activity, especially white collar crime. Greed and other features of human nature apply. The days when politicians were absolutely untouchables when it came to these kinds of crimes were gone with Kamuzu. He and his coterie were really heavy on tax evasion: they practiced what could be termed reverse taxation, whereby they actually took money from MRA – who knows how much, since there was NO accountability. Businesses have to pay their share of taxes, rather than leaving the heavy lifting to you and me. MRA are just doing their job.… Read more »
Witch huntinging by nervious Diesel, Ptrol, Palibe. Muwafune woti mungawaopsyeze