Email a copy of 'Malawi to introduce paying fees in hospitals -Minister' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

128 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Napofu
Napofu
9 years ago

Pokhapo ndiye mwaonjeza.Anzanu sanafike pamenepo.Anthu akumudzi ndi ovutika kwambiri .Ndalama ayitenga kuti? Chimene mukudziwa inu ndikufuna malipiro ambiri mukapita ku nyumba ya malamulo.Mwayiwala zomwe mumanena pa kampeni nthawi ija.Ngati zakukanikani bwerani poyera ndi boma lanu lobelaro.Kamuzu amkadulitsa makadi ndalamazo ndikumayendetsera chipani.Komanso misonkho ndalama zake zimagwira ntchito ya boma.Ngati zili choncho ndiye ndibwino musiye kutidula misonkho.anthu akuba inu.

Feeling very sad
Feeling very sad
9 years ago

Its really sad looking at some of the comments on this forum. It makes one think if Malawians have brains at all. I don’t think anyone commenting on this story is from the village or so poor. Probably most go to private clinics for treatment. Malawians lets think before we type. The Majority of the population are very poor people, these are the poor that visit hospitals. Its easy for a Minister to stand some in the midst of a huge crowd and advocate for fees at the hospitals. How many of these even go public hospitals. A lot of… Read more »

Lupanga
9 years ago

Ine ndi brain yangayi sindibakira zopusa koma mantha okhawo ayaya ayaya ayayaya!

zangaphe
9 years ago

Uwu nde umbuzi weniweni boma muganiza kuti anthu akapeza kuti ndalama zoti azilipila chonsecho tili pa number 1 umphawi zazii agalu inu.

Hoitty
Hoitty
9 years ago

Koma anthu osauka akumudzi amakondanso kupita kwa sing’anga ndi a zamba. Kumeneko amakalipirako

Chimwamowa
Chimwamowa
9 years ago

Tingomenyanamo Muno Basi

Wodzichepetsa
Wodzichepetsa
9 years ago

Tikumane ku nseu basi,,

DPP kusanva~ muziwanso

edda mwalweni
edda mwalweni
9 years ago

apa ndiye yalakwa!

Yuri
Yuri
9 years ago

Also introduce a free coffin workshop!

musovenge
9 years ago

u ll solve kuumilira kulamula Mulungu asanalore lero ndizimenezo mukufinya anthu osauka omwe anakuvoterani kuti akupatseni ndalama zoyendetsera boma

Read previous post:
Lack of staff hampering functionality of Mzimba eye clinic

A K100 million kwacha eye clinic in Mzimba district is not yet operational months after completion, reportedly due to “some...

Close