Email a copy of 'Maulidi claims backing from PP brass against JB ' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Maulidi claims backing from PP brass against JB ' to a friend
Malawi Government through its Chief Information Officer John Chilikizo has defended government's decision not to table the Access to Information...
Bena mphoto mose ndimwe vindere vyakufipo.nadi hule la chanakazi limupusikaninge, imwe nadi matongo lende kuti tiyeni tiyeni tiyime pathekha.aah ndimwe vizeleza!
koma ngati mulumana ndikudyana chenjerani mungapwetekane
If MEC failed,it was PP’s ineffectiveness on it as a state body.Funding was very poor,logistically nde worse,analephera kuwapanga empower mokwanila for tripartite elections.
Wina amati aMaulidi munangoti akhale pampando,basi kukanilira.Owowooo,kuterokoo.
Anaonera abiti maloko,nawonso kungoti khalani apa yiiiiii,mpaka kukanilira kutsala pangono kuyambitsa nkhondo.
Anthu tisamakonde kukamba za ena coz sitiakonda pomwe nafe tikupanga zomwezo.Taonaninso shadow cabinet ya MCP,koma bwanji kukuwa kwake ndi ya DPP.
Tiyeni tinene chilungamo pa chilichonse,sitimati God Fearing Nation.
PP first lost its vice president central due to political carelessness. The party was quick to dismiss him as lazy and useless. Then it lost its vice president south and then North. The party took it easy. Came elections the party got a third position and blamed MEC for that without doing any serious soul searching. Now the party is repeating the same blunders by standing on the way of the very people who want to hold up the reputation of the party on the ground through participation in the by elections……
Does this party learn from its past mistakes.
Pipii ! kenako odi uko! chipani chuukagwa! hutale siyuliranso odi uko!!!
Maulidi wachita boo. Asiye abiti lock ndikulephera kwaoko asati akuletse iwe. Iwo anapikisana analephera pa 20 May paja, iwe ndi ufulu wako kutero uwone kuti ulephelera pati. U don’t trust MEC because u failed. Ngakhale kukokerako no 3 iiiiiiii abale inu, ati mukati boma sililuza taonera inutu.
Maulidi pliz stop this unless if its a stunt
MAULID, MAULID, is a complete political FAILURE! He was in UDF, failed. In st. DPP failed. MChipani ndi boma la amayi athu, he failed. Then anangomukokera kuti akhale Acting SG ndiye akaupanganso makani. Inu, a PP Musiyeni ayime pa zisankho. Ndipo alephera. Koma chonde akalephera musamulorenso mu Chipani chatu. Akayambe chake ndi mzake failure wina ” his excellency Chenji goro Uladi Musa. president wa chipani cha anthu awiri. Asaaaaaaaaaaaa. What a couple!
Akunama amaiwo, a Maulidi kapikisaneni. Nseu wa Lirangwe Chingale mpaka ku Machinga kuti utheke pakufunika anthu ngati inu. Please do not give up. Ken wa chinkhope ngati nyani kapena amai oyenda ngati bakha sangabwelese chitukuko kwanu koma inu basi. Maulidi yemweyo koma kuti wa wa wa wa wa wa !!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Kayambe Chako chipani iweeee tione ngati ungathe!…pew pew pwe za ziiiiiii MEC ndi mbava Zokha Zokha we will never deal with that MEC unless we are idiots like you!