Email a copy of 'MCP demand names in Malawi UN entourage: CHRR, Cedep add voice of concern' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

52 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Okay
8 years ago

But this larger than life size portrait of Chakwera. Or is he standing up? Koma the heart does not put on rugs indeed! Kuteroko akuti kuzimva kuti ali ndi authority, kuiwala kuti real authority ndi ija adaithawa pa pulpit ija. So a friend of mine Elias has joined this game of fools!

clement
clement
8 years ago

Ngakhale mutadziwa maina mungachite chiyani amphaka ngati inu? Ngakhale kuti anthu avote mawa DPP iwinanso inuyo mukhale chete DPP ikonze dzikoli. Mwalephera kupanga za nzeru zaka makumi atatu kuchita kulephera kuika nseu Ku ntchisi ngakhale pa kamphata pomwepa kulephera afisi inu. Lero DPP yayamba kuwalitsa katauni kanu kafumbika mwayamba kusukusula. Bwanji mulimbane ndikulima Ife tizigula kuti muzipeza yomwera tea paja inu ngakhale kutenthe tea ndiye simuleka azimwale yooo.

Nebraska
8 years ago

Noise noise and noise opposition and groups fooled by MCP and Jessie. Koma zakhala bwino mwaiwalako za in-house-fighting with Felix Jumbe amuna bambo. Osati ozilemeretsa pobera osauka potolera zambale mkachisi!

the truth
the truth
8 years ago

MCP needs truly to re brand and stop politics of hearsaysor hear some put your facts straight. The nation needs your evidence on the bloated entourage why relying on gossip.

Chita
Chita
8 years ago

The names have been given, so what MCP? Ndiye mutani tsopano? Go and hold another press conference. A party full of press conferences but no rallies. KKKKKKKKKKKKKKKKKK

The Most Concerned
The Most Concerned
8 years ago

Whatever the number APM has taken with him to UN, we already started yielding the results. USA has given Malawi K9,000,000,000.00 Grant for food aid, ndiye mikuti chani? Continue buying favours from Malawians, ife dziko liri m’manja mwathu ili.

Zebede
Zebede
8 years ago

MCP and all opposition parties, CSOs and other economic and human rights organizations- you are actually sleeping while on duty. You are not helping Malawi and Malawians. Have you removed the words “proactivity, vigilant” from your vocabulary list? This govt and other previous govts have taken advantage of such weaknesses and have done very displeasant things to Malawians. May I therefore urge you to develop very watchful eyes and alert minds. Let’s make noise before worse things happen. Some legislation may do

kaliati
8 years ago

umbuli panyapako kumwera ndekut chan…u dnt c any point nyapapi iwe? do u wrk retard iwe…

Chinena
Chinena
8 years ago

Mbuli zachilomwe zisiyeni zovotera chibekete ngati ichi

George Kamanga
8 years ago

Inu a Malawi muzingopemphera mmene munachitira nthawi ya galu uja bingu.

galuyu (APM) musalimbane naye tsiku likwana. zawo za nthawi yochepa.

Mulungu akumenyerani nkhondo mukakhala mwa iye muchowoonadi ndi chilungamo.

Read previous post:
Don’t take Malawians for fools, Chakwera tells Mutharika govt

Leader of opposition and Malawi Congress Party (MCP) president Lazarous Chakwera has accused the ruling Democratic Progressive Party (DPP) of...

Close