Email a copy of 'MCP, DPP put primary  elections on hold over  UTM  momentum' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

28 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Odala
Odala
5 years ago

Thats what we call politics bambo. They want to put UTM at the corner.

Kaisala
Kaisala
5 years ago

MCP thought kuti it has found those disappointed supporters from DPP. Munangoona Chilima tulukiro anthu onse balala. So desperate. Kubwera Mia basi kusokonezeratu MCP in actual sense he seems to be the President. That’s the Mia i know. Chipani cha nyau sichidzawinanso

Kaitano
Kaitano
5 years ago
Reply to  Kaisala

Koma man,gwilitsani ntchito bwino ufulu wanu, musaononge kapena kunyoza azanu pa chikhalidwe chawo,inu chipani chanu ndi cha afisi, ndi fiti zotamba masana pa nyumba ya Patricia Kaliati komaso kugona ndi tiana pofalitsa matenda ya Edzi. Ukuva bwanji pamenepo?

mark
mark
5 years ago

CHILIMA IS GOING NOWHERE

MUNYERA
MUNYERA
5 years ago

Mukambekambe mmene muthere koma kumapeto a nkhani SKC BOMA. Mmene tinkafotokoza mu 2014 kuti chipani cholamula chiluza anthu anatikamba izi ndi izo, what happened? History repeats itself. You really dont need to be a parachute scientist to understand this, SKC is winning come 2019 polls. Amene mukuti kumudzi sakumudziwa Chilima iiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii mwauponda, ife timakhalira kuyenda mmidzi throughout the country and imvani zomwe mkambazi. Enanu kaya ndimantha kuopa maula prison, zanu simukadya ndiife koma choti mudziwe Chilima wavaya basi palibe amupeze. MCP mutsogoleranso kutsutsa ndi momwe ziliri. pano ndili ku Phalombe. mawa ndikhala kuchikwawa koma dzulo ndinali ku mwanza ndi neno.

Kadzakumanja
Kadzakumanja
5 years ago

Chilima akuti tatopa ndi kuona azimayi akugwedeza mbina pa misonkhano,mmalo moti adzikasamala ana kunyumba mukuwatengera kumisonkhano kuti adzikagwetsa mapadi pansi…ena amasangalala ndi ma pad wo, ndiye sakumufuna Chilima…mudzaone msonkhano uliwonse wa andale ukatha, sipalephera kupezeka pad yogwetsedwa pansi. Wina akuti iyayi, UTM iyayi tikufuna tidzionabe ma pad. Mankhwala kapena chani? Dziko lokupsa ndi dzuwa ili. Apatseni ulemu wawo azimayi oyenera.

santana
santana
5 years ago

Chilima’s equal is Atupele. I even doubt if his votes will be more than those of ATU.

Kadzakumanja
Kadzakumanja
5 years ago
Reply to  santana

Keep dreaming! You will be shocked.

Ambele Kwacheni Banda
Ambele Kwacheni Banda
5 years ago

DPP and MCP kusamva these parties have already names they want for primaries and anthu aiwelenga kale ndiye
they want mutenge anuwo then otsala azaima UTM or independent.

Kaitano
Kaitano
5 years ago

Sizoona zalembadwazi, the MCP you are talking about can not and will not be shaken with UTM you are talking here man, it has been there fighting for Malawians, some of you like Winston Msowoya are people who are not civilized, MCP is now not a Party it’s now a basket of hope under Chakwera and Mia, ngati tinasintha masankho a NEC why can have a panic kusintha ma Primaries? UTM is ababy for DPP not MCP, zipangani phokosolo zanu izo, the problem is that we have many idiots in this Country.

Namalomba Fredrick
Namalomba Fredrick
5 years ago

Zilubwalubwani UTM, UTM ndiye chani???? The only good thing about Chilima is his age, he is a crook and surrounded by disgruntled former DPP & MCP members, a Malawi simuchedwa kuyiwala. If he was allowed to stand as a DPP presidential candidate next year, do you think he would have left and be talking bad about DPP??????????? If Patricia Kaliati was a Minister do you think he would have been in this movement. If Richard Msowoya was to be made Chakwera runningmate in 2019, do you think he would have left it?????? A party which made him Speaker?????? A Malawi… Read more »

SIBODZA
SIBODZA
5 years ago

Precautionary measures is good politics not the prescription offered by the arm critics in the holy name of analysts. Practical reading of the unfolding politics is in the hands of the parties therefore the interpretation is theirs. Our analysts in the academia are a pile of trash they tend to thrust their half researched opinions on the readership especially Hussein from Iraq university you read blue lines in his commentaries

Read previous post:
Political parties defend their record on promotion of youth

Major political parties in the country have all said they are doing very well when it comes to promotion of...

Close