Email a copy of 'Miss Malawi to be crowned tonight: 14 beauty queens to contest' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Miss Malawi to be crowned tonight: 14 beauty queens to contest' to a friend
Minister of Information and Communications Technology Nicholas Dausi has denied accusations by a group of civil society organisations (CSOs) that President...
Gladys Kumbatira is not growing. In October, 2011 when she was dating Mnthumwi Pisky, she was 20 years old while studying at MCA, six years later she has only added 4 years. Koma yaaaaaaa!
Amenewa ndiye mukuti akazi okongola ,kaya mphanda zinazi ndiye mwazitenga kuti.munthu kuonekeratu pojoina myendo looo !!jamani !!!! mbala sizingavutike ndi anthu ngati amenewa ma expand awo ndi otsegulatsegula kale No problem .
All the best, let the best of the best carry the day
kod akazi okongola ku malawi kuno anawaletsa kupikisana nawo pa uchiphadzuwa wa kuno ku malawi ? zimandidabwitsa kuti akazi omwe amapikisana nawo samakwanila kukhala miss malawi. zoona matupi amenewa azungu aziti ku malawi kuli njala yosatha ya mgonagona ndiye bolanso kutenga anyani azipikasana akhoza kumakopa alendo langa ndi pempho muganizilepo bwino
CV ya Nthanda ndiyowinawina kale 90% kwangotsala 10% yoti akokele ndima looks,catwalking and speech. I’M FOR YOU
Competition is btwn yvonne n thanda ……
Akuchitani ndithu
Koma ku Malawi komvetsa chisoni ndithu. So these skinny shabby looking girls consider themselves beautiful? Pitani mukaone pa Nairobi, Maputo, South Africa, Addis Ababa ndi Lusaka.
@Le Cologne – Ndiye ukufuna akazi aku Nairobi, Maputo akowo azakhale miss Malawi? I bet if you have a girlfriend/wife, she is Malawian kkkkkk unagwira onyansa!!
Akulu pathako panu…..Kuno ndikuMalawi!! Zakumazambiki zanuzo kagwele nazoni uko!!! Ife zathu ndizimenezizi….asafuna asiye
anthu samakhala ofanana brother,