Email a copy of 'MP Menyani denies DPP link, says Malawi future belongs to MCP' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MP Menyani denies DPP link, says Malawi future belongs to MCP' to a friend
The Balaka Second Grade Magistrate Court has set free a 34-year-old man who allegedly chopped off his friend’s fingers. Police...
Inu monga simudziwa kapena you are still in the denial stage? Can we can we really call these thieves leaders? Imagine Muluzi = 1. 7 billion kuba mlandu uli ku khoti. Amayi = Cashgate. She is in hiding. Pitala = 92 billion kwacha= MSB stealing through selling. Amenewa ungati atsogoleri kapena ambanda/mafias?
The future of anything lies in its inception. If you destroy the begining you have destroyed the future. So Menyani is right to say that the future of Malawi is indeed the MCP.
umaitha menyani agenda katauluka we MCP forever!!!!!!!!!!!!!
that is true imaraan sadick tamavomerezani zinazi.
Menyani yemweyo kuti wa wa wa!
Ungalowe DPP iweyo? Kuti chani? Akulodza ambuyako?
Ulowe DPP kuti uzikatenga misonkho nkumalipilira ngongole za akathyali?
Kuti uzikaba ndalama za NAC?
Kuti nankhumwa akakupatsire chiwewe?
Kuti uzikalemba grafiti?
Yayi tele……Menyani wathuwathu uyu!
Where did you get that nonsense that the future of Malawi lies in the hands of MCP Mr Menyani?
By the time you Menyani realises that you are wrong and MCP will not govern Malawi in near future our offer would have expired. You have very limited time to make a wise decision otherwise we will be consulting our next candidate Juliana Lunguzi
Following
Kodi Sosten Gwengwe alipo? Ali ku Malawi komweku kapena akuthamangathatha kunjaku ndi a Mayi? Paja ndi running mate..,
nilibe chonena poti mwanayu ngwanga