Email a copy of 'MPs shocked with malnutrition levels in Malawi caused by food shortages' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MPs shocked with malnutrition levels in Malawi caused by food shortages' to a friend
Outrspoken Member of Parliament for Mzimba Hora, Rev. Christopher Mzomera Ngwira has repeated calls that the country should have a...
SCO —-ECD k327 million ya NUTRITION– koma zilipo. pano nde mwagundika mungoti kathumba ka cimanga, etc ati kusangalasa anthu pa xmas.
mmmmmhu
all these bastards is feasting basi. aliyese akuziwa. awa sikuti sakuziwa za anthufe njala mmizi muno ai, angotseka mmakutu basi. palibe amatambasula dzanja koma luting basi.aliyese amawaona tangoonani mimba zao. masaya, mbina za amuna. maonekedwe amatiuza zambili.apa angofuna ma alawasi.
anthuwa tikawasankha basi mooto wa ku town kukayamba ma plan oyamba ma kontraki business.kupasana ngongole zosazabweza. ena ngongole zomwe anatenga nthawi ya kamuzu, muluzi ,bingu sanabwezere. kkkkk ma TRUCK. zikomo
were funds given and badly utilized?
But how can MPs be shocked when they actually stay with the public? Nde
kuti iwo amangodya okha? What actually do they report to Parliament only
to be shocked after reading a report in suits?
Malawi a failed state indeed
Yet one so called professor says no one will die of hunger this year. Malnutrition is
is the after effects of hunger. There are many deaths caused by after effects of
hunger . Learn to tell the truth rather than hiding your head in the sand.