Leo!! Ma Players Take Care Amamenya Makofi Amenwyo.
clement
9 years ago
Zili ndiwe Leo kupita kapena osapita koma ndikanakonda ukanakhala ku BT united cholinga ibwelere msanga ku Super League.Pano sizikunditsangalatsa matimu atsala ochepa kumwera kuyerekeza ndi pakati pamene mbuyomu kumwera kunali matimu 8 lero 4 enieni eeeish.Think twice Uncle Leo
Honestly,epac Has Goofed Coz Mpulula Is Not Fully Recovered, U Know Futbol Needs Alot Of Thinking And Fitness,
Leo!! Ma Players Take Care Amamenya Makofi Amenwyo.
Zili ndiwe Leo kupita kapena osapita koma ndikanakonda ukanakhala ku BT united cholinga ibwelere msanga ku Super League.Pano sizikunditsangalatsa matimu atsala ochepa kumwera kuyerekeza ndi pakati pamene mbuyomu kumwera kunali matimu 8 lero 4 enieni eeeish.Think twice Uncle Leo
A Reo bwelani kuno mudzatukule mpira Ku capital.