Email a copy of 'Mtakataka community secondary closed indefinitely' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mtakataka community secondary closed indefinitely' to a friend
American Energy Company has committed to establish a plant in Malawi by 2016 in order to reduce power deficit hitting...
Let’s not just judge the students as always wrong. Yes Head is educated but some heads are there because of promotion and drug not because of academic papers. Such heads have inferiority complex and as a result they indeed facilitates transfers of highly educated teachers in the name of “removing opposition”
ana opusa ngati awa sindinawonepo coz akulimbana ndimunthu woti zake zinaye koma know this simupindura a head she smart i know her anali pa mlodza but now ana anawadandawura atachoka dec sikupindulirani a head simunarakwitse try to forgive them,,,
ana opusa ngati awa sindinawoneposo ahead ndimunthu woti anapanga zake kale nde u must know kuti ahead alibe udindo ochosa mphusitsi pa xol, i know her a mati akafika pamalo pamasitha chitukuko komaso ana amakhoza bwino for example anali pa mlodza sec xol, ana pano amawalira so musaseweretse mwayi dec si xul yoti bwaj,,,,,,,
Kusadziwa ndi kufa komwe ana inu konzani zamoyo wanu osati kumavutitsa makolo kusaka fees inu mkumapangaso zopusa umeneu ndiumbuli
Achidongo mwangozitayila ulemu wakunyumba kwanu, kapenatiti achidongo ophunzila anapita ku univesity. Aliyense alindiufulu osankha schl yimene ili afortable Dec inalibwino kwaana aamphawi ngati ife. Ndiye tisaphe sogolo laana ndichifukwa chandalama achidongo!
Chidingo John,you are right that gvt gives litle attention to CDSS/Dec,I am proud to be one of the products of CDSS,but there are some smart students in CDSS than conventional secondary schools,because of Quota system,when I met the guys who were in boarding schools,I was like what? This world fabours some low IQs indeed,ufiti weni weni,so don’t talk too much trash of CDSSes
Ana inu ndi mbuzi Za mapeto. Head is educated
Ana inu ndinu womvetsa chisoni ndipo ndinu mbuli mukuona ngati Dec ndi school yoti muzivuta nayo ngati muli school yomwe inalengedwa kuti muzingotailako nthawi kuti mukule ndiye Dec. Ndi angati Ana aku Dec amene sankhidwa Ku pita Ku university. Ndi angati amene Ali mabwana Ku makapani. Pa maufulupo akuti muzisankha aziphunzitsi. Or atangotsekeratu mutipindulira chani Malawi muno .chizungu kulemba kuwerenga simudziwanso. Chosecho makolo amachita Ku vutika ndi fees. Kulembani ntchito ndinunso mumayambitsa ma stilaka ngati amenewa. Dec is to pass the hours away ndakumasurani chilungamo kuwawa.ngati kuli school Ku secondary level imene boma silikirako nzeru ndi DEC. Joe tiye tikadye… Read more »
In the first place the headteacher is a woman,then do more research before publishing inu a NYASI TIMES. please!!
So form four examinations have been scraped off.