Email a copy of 'Mulhako wa Alhomwe to spend K100 mil for 10th anniversary' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mulhako wa Alhomwe to spend K100 mil for 10th anniversary' to a friend
Parliament’s Public Accounts Committee (PAC) chairperson Alekeni Menyani said state produce trader Agricultural Development and Marketing Corporation (Admarc) is being...
Penapake tiyeni tiziika umunthu patsongolo K100 million kupezeka ya chimphwando koma nzipatala makhwala kulibe amalawi tazipangani zanzeru kodi ndalama zimenezo mutagulira makhwala muombola miyoyo ya amalawi ambiri.Utsogoleri wanzeru umaika zofuna ndi zothandiza anthu ake kunthawi zonse Mulungunso azakupatsani nzeru ndi madalitso ochuluka.
Ndalama zaku ESCOM zimenezo. Zipatala kusowa mankhwala koma alomwe akumwelela. Dziko lavunda ili.
WASTING K100 MILLION WHILE THEIR CHILDREN CONTINUE TO LEARN UNDER TREES. WAITING FOR DONORS TO HELP THEM .DO WE HAVE PRIORITIES??? THIS COUNTRY IS CURSED FOR SURE.
Anthu okhulupirira zopusa zopapana magazi.
Why do you speak Chichewa at this function? It is a dead tribe. Shame on you.