Email a copy of 'Mutharika leads Remembrance tributes at Lilongwe Cenotaph' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mutharika leads Remembrance tributes at Lilongwe Cenotaph' to a friend
Police in Malawi’s eastern district of Balaka are keeping in custody a husband and a wife for allegedly neglecting to...
These people unfortunately died for the British crown and not Malawi as it is being reported. Those wars had nothing to do with Africa and black people.
Chakwera is a good man to those who dont like him just shut up your mouth ulemu anaperaka or umafuna agwade kwa Pital wakoyo
Ambuje ku lilongwe
Munapambana masankho pobera
Results= mukulephera kuyendetsa dziko. Miyezi 5 yokha zinthu zasolobana.
Go on the street and kamvetsereni zomwe anthu akunena (including iwo amene anamuvotera mkuluyu).
Chifukwa choti mukudya nawo zamuseri mwaona kuti onse amene ali ngati inu? Rubbish.
Abale koma abusa kulephera kupeleka ulemu kwa president wa dziko mkwiyo omweujabe udakalipo? Osangokhala bwanji osapita ngati simufuna kulemekeza mtsogoleri wa dziko? Kukula mtima kumeneko ndiusogoleri sizikanagwirizanatu. Zinakhala booo kuti munalephera pacisankho. Simumaona zomwe amapanga amzanu pamenepaja. Ndipo pa 2019 muzalephera kwambiri muzacita manyazi ngati simuzicepetsa.
Ulemu sitipempha nawe…. Tiye uko.. Kukamwa anga chona…
Ma CIVIL SERVANTS SANALAMDIREBE MPAKA PANO.
Ndiye mumati katangale malo ngati ku immigration atha bwanji? Adya chani pa tawuni?
APATSENI ZAWO. MA BIZINESI ATHU DEPENDS ON THESE PIPO.
Koma has this anything to do with poverty reduction in the country?