Email a copy of 'Mutharika to preside over installation of controversial Kapoloma chieftaincy' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mutharika to preside over installation of controversial Kapoloma chieftaincy' to a friend
Malawi Vice President Saulos Chilima has commended smallholder farmers in the country for their role they play in agriculture and...
CONDOLENCES TO THE FAMILIES OF THE 9 NINE POLICE OFFICERS WHO HAVE DIED ON APM’S CONVOY AFTER THE FUNCTION
Go on Peter!! Ngakhale munyoze president mungovutika ufumu uvekedwa basi mfitinu mung’omboka m’maso ndi majerasi anuwo. Kani pakhomo pakakhala njala bambo sayenda? Mudzichita ngati munapita ku sukulu osamangolowetsa ndale zilizonse.
Ameneyo nde Bakili. Inu m’maona ngati pofika Kamuzu kumuika secretary general wa MCP anawona chani mwa Bakili? Mmene uzizandikira APM kuchenjera kwa tate limeneli uzakhala uli chagada. Mark my words!!
Number 9 a court ngati anena why is it that the concerned parties at the Centre of controversy know nothing about the court ruling? Fatsani mumva wina ataon zakuda
What do you expect from z controversial leader?
iWE PETULO UNKANYOZA JB KUTI AKUNGOKHALIRA KULONGA NDI KUKWEZA MAFUMU. NAWENSO LERO WAYAMBA ZOMWEZO? BULLSHIT PRESIDENT
Peter Mutharika must just resign.Ntchitoyi yamukulira.Malawi realy on autopilot.
Apa zachidziwikile kuti APM akufuna kusangalatsa Chair. Why waste money kukaonela kulonga ufumu when the country is facing economic hardships? I thot ndi Ntchito ya Minister of Local Govt. Koma zilipo ku Malawi
MTHALIKA MUST CONCENTRATE ON REAL MATAS IN MW NOT THIS.PETER COME OUT FROM YO COCOON ANDSORT DE MESS AT JUDICIALY
Kodi mukufuna APM aweluzenso nkhaniyi? mesa akhothi anagwilapo ntchito yawo . Anthu ena mumakhala ngati anzeru koma muli mbuli. Wina akuti kupite chilima kumeneko mwayiwala kuti ndi udindo wake president. Kumazitsata zinthuzi APM akungokwanilitsa iye angatani ngati akhothi anena