Email a copy of 'Mzuni beats Moyale in Mzuzu derby: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mzuni beats Moyale in Mzuzu derby: Malawi TNM Super League' to a friend
Malawi national football team, the Flames , on Sunday lost to Zambia’s Chipolopolo 0-2, the first defeat against their neibhours...
Thanks Mzuni you really made us happy. Iam proud of you. Tell the spin doctor from zodiak uja amfuna tisalowe mu TNM Superleague akumva bwa? Nda kuti iyeyo amasapota Kasungu Polisi. Kaya idzalowa lit imeneyo mu TNM. Tikumva kukoma. This what we call ontological football if philosophy but quantum football is physics. Ndapita. I hop towochaso kafuti kenaso kabwera pa 24 pano.kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Kalambula bwalo wake kukhala Airborne Rangers pa 24 may apa. Chonde bweraninso kut mzaone kukonzekela kwake Mzuni yomwe yabwera kuzakhala mu TNM Super League. Winawe zikuwawe popeza unayetsetsa kuzera mwa team ina kut tisalowe koma hii! University, yaonetsa kuganiza kweke, kkkkk kkkkkk he he kkkkkkkkkk
Mzuni yomweyo !! kuti wa! wa! wa!! bweraninso pa 30 may kut mzaone Mzuni ikuimitsa Borring Bullets! oooooyo!
enhee-e!! olimbana ndinefe, mu2meninso reporter wanu pano
Ma Intellectuals ndipa ground pomwe enanu muziona.School yathu apa timati yayaka
Bravo Mzuni
Titalikitsireni adani last season amatilondalonda kwambiri amenewa shaa koka! Timababy tavuta nato ta mBlantyre tayambapo “Barca” ya pa Malawi yasisimisa mikango dzuro.
thats what in academic we call Calculus Football or Algorithmic Football passes, osat zanuzi. Mzuni, teach umpira
Sukulu si manama. not SIMAMA conflit.
When the hunters learn to shoot without missing,the birds also learn to fly high without landing,,,,,,,,,,,VIVA MZUNI,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,Neba zamuvuta