Email a copy of 'Ndawa tells Nyasa Bullets fans to keep calm' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Ndawa tells Nyasa Bullets fans to keep calm' to a friend
Ministry of Agriculture, Irrigation and Water Development has warned people of Karonga District of more rains which may result into...
its only the first game out of thirtty.keep quiete you chartering nebas.
kkkkkk sunday ndikuonanso mdima kkkk coach usamale imeneyo si team yokhalako poti sunday zikakuvuta basi uli mmadzi ha ha ha ha ha
Tidikira Zabwino This Week
zandibowa,mpakana draw.
Bullets executive to blame, said many times before that Ndawa is not yet a Men’s football coach koma kukakamira a Tewesa n Chilunga.
If we dont win on sunday then the coach n executive must GO!
ZOMALEMBA MA COMMENT OPUSA APA AYI MUHAMMAD SULUMBA SANGALEMBE ZALEMBEDWA APAZI WELEMBAWE NDIWE WA NOMA MWANA WA BUTAO KAGWERE UKO UFITI BASI KUZOLOWERA KUGWIRITSA NTCHITO NYANGA ZAKWA AYAYA A KUBALAKA SHUPITI!
osadanda ma pale zinthu ziyenda bho bhoo
Koma zoona ndithu ntchito sikukhala ndi pepala. Bola Mavuto Lungu. Nanga kuyamba ndi minyama chonchi? Kenaka mmalo mopepesa kumanena kuti anthu akhale chete? Kodi sumadziwa kuti Bullets ndi Timu ya anthu (Peoples team)? Wake up and fix this Sulumba boy.
Pepa Neba……………Mavuto saona nkhope….!
Ine muhammad sulumba ndikumachitala dala ku phonya ndatumidwa ndi neba kuti ndisokoneze bullets ndipo munya simunati