Email a copy of 'No dignity in death as Malawi women forced to carry dead body of child due to lack of transport' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

7 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
NYONYO
NYONYO
7 years ago

hahahahha amalawi boma likudyetseni, likukumbireni zitsime akumangileni nyumba hahahah mpaka maliro inu udindo wanu ndi chani? hahahahaha hahahahah mwaonjeza

A gama
A gama
7 years ago
Reply to  NYONYO

iwe, ntchito ya nsonkho womwe akutidula ndi chani? pali kumanga zipatala ndi ma schools, providing security services ku dziko osati zomwe ukubwebweta iwezo!!! ndekuti ma ambulance muzipatala ayeneka apezeke

zuze dekha
zuze dekha
7 years ago

komatu iwo akafa ma helokopta ,cimzere ca magalimoto, tinena thoo. akati ophikila anthu wamba nde ndiife akumudzi, okagona ku malilo ndiife, am sure if each minister could give away one car olo the money to buy the posh car was given to a district, yes each district would hve an ambulansi. zitha kutheka. koma ndi mmene zililimuai ndithu. poti akadzafa mabwanawa adzatenga cumaci.am sure kuti anthu tikanamaganizila za infa pano sitikukuba motelemu.
mwina timaba kudyelatu kusesa kuti obwela asazapeze kanthu azayambe yekha. kuphwanya kugulula ziseko mawindo kuthothola makatani. kkkkkkkkkk eish anthu ndife oopsa tisamangoonana. ndangodusamo

Panganja
Panganja
7 years ago

This is today’s Malawi run by Mathanyula. Shame on he who is the so called leader of Malawi.

zuzo dekha
zuzo dekha
7 years ago

izi pano zitatha kalekale, tili ndi anthu tinawasankha otiimilila za mavuto?zabwino zomwe timakumana nazo mmamizimu, but are thry doing?? kusankhidwa basi wa ku town kuyamba ma business ndi ndlama za citukuko ca mmidzimu. ma galimoto poshi cars kumpanda kose thoo.anthu a kumizi anazizolowela cifukwa palibe angawathandize. ma ambulasi ali mma bomamu ndi okatutila matumba a cimanga, makala, nkhuni, matumba a cement etc za ma bwana a mma district. fusanai ma driver ndiomwe amadya bwino. kanani

Sailota
Sailota
7 years ago

Yet someone is bussy in ….gate. Shame. Zonse nzotsala, ask the late…..

benjones
7 years ago

Shame on the Rich Society who continue to seal from the poor.

Read previous post:
Pop star Rihanna meets Lilongwe Girls Secondary school students during Malawi charity trip

Pop globe super star r Robyn Rihanna Fenty travelled to Malawi on behalf of her Clara Lionel Foundation and on...

Close