Email a copy of 'Nomads seek divine intervention at Catholic church' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nomads seek divine intervention at Catholic church' to a friend
In bid to continue with the breast cancer awareness , Think Pink Malawi organization has advised women in the country...
god will answer our quesions
what is the story here,in everything to ask God intavation is good the only problem we expect feedback fom God same time but if u continue God answers u differently and in another way.what they did was not bad it was already sunday. keep up everytime be doing that even not winning God protect us from crucial injuries.
My foot kulankhula kwambiri mpira usanayambe. M’mene mumapemphera masapota any ama tuzuka m’muzimu. Ndiye kuchalichi munankako munakamwera zikho za YAHWEH lero dzanja lalemba.
Iwe number 9 ndiwe wotemberedwa kuchokere kwa makolo ako wamvapo ndani akunyoza apa nawe ukuti mpingo wolakwika ndiwe munthu uli desperate ndi matchalichi ampatuko uli ndimatenda eti?
Mulungu samasewela phada, chipako kapena mpira wa miyendo. Chonde osamamuyesa dala muzaputa nazo mkwiyo wa Yehova. Tawonani lero Mulungu wapeleka ukulu wanu kwa Kandonje.
munatsogoza kulamula Mulungu ,shaa plan ya munthu amadziwa ndi mwini sachedwa safulumira kkkkkkiii
Pano a Midiera muti chiani? zabvuta basi pepani koma matama musiyeyeyeye
Pepan pepan,nkhani yavuta kwa neba ndi chikhulupiliro, mulungu ngolola chirichonse kuchitika.pankhani zandalama neba usamale ndimulungu. wamwa dzana munamuiwala ndiye mumafuna akupatseni ATM CARD..MUkanamkumbukira mulunguyo.
Good decision! Wrong congregation!
Panali nzelu kwabasi pokapembeza Yesu okhala mu Ukalistiya.
Koma nkhani ndiyoti this country is broke so nkhani ya ndalama tizigawanako wina Carlsberg Special, wina ATM card and finaly TNM airtime BB woooooyeeeeeeee.
Zikamatele tele tele mnzosowaaaaa.