Email a copy of 'Nyasa Bullets mulling over transfer targets' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nyasa Bullets mulling over transfer targets' to a friend
Mighty Be Forward Wanderers and Flames midfielder Isaac Kaliati is expected back home today from South Africa where he went...
bobobo executive yathu pano tikufuna kutola zosalira kwa neba shaaaa zandinyasatu kkkkk
bullets koma kugulisa ngambwe basi aaaaaaaa ngati angamake 2017 alimbe kkkkkkkkkkk
i think kondie ndiyekhayo adaithandizako bullets
.. sizinazadyeraziyi…
kkkkkkkkk bullets inazaza anthu a dyera kugula player amaona kuluza moti apa akudikira zomwe ataye a Noma kuti atenge
We shouldn’t blame the chairman or the executive but the supporter we were busy fighting among ourselves while our friends (nomads) were busy negotiating deals with the players…
bullets kugula prayer zimavuta kwambiri chifukwa cha dyera chairman wathuyu .munthu uzidziwa choyenera kuchita osati bobo ai zandidyasa kwabasi.