Email a copy of 'Peacock donates seeds for winter cropping to Salima farmers' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Peacock donates seeds for winter cropping to Salima farmers' to a friend
The Lilongwe High Court has set the last week of the month of June as the tentative day presiding judge Blantyre-based...
Nanga iwe nzanga Bwande udamvapo kuti Chakwera kapena Jessie kapena Msowoya wagawapo zinthu zaulere? For Msowoya zomwe ndinamva ine ndizoti adathawitsa chibwenzi chake Jessie Kabwira ku Parliament kuti asamthire nawo unyolo penanso ndidamva kuti adamtuma nfana wina wake kukaba ” mfuti ” ku Capital Hill basi!
Tiyeni nazoni. Sikuti ndizolakwika. Koma penapake pakundiopsya makamaka zomaona kuti mtsogoleri wabwino ndiye kuti ndiamene akugawa zinthu zaulele. Komabe popeza ndimmene tinadziwira democracy yakwathu kuno. Atcheya anawononga zinthu. Ukuwona bwanji bwanawe
Apa pokha pastor Chakwera sangamake. Jumbe ndi mitunda ina iyi. MCP cannot defeat him.
Koma man Jumbe ku MCPko kukanakhal anthu anzeru ngati inu atatu kapena asanu chipani chanucho sibwenzi chikuchititsa misonkhano kwa anthu kuchuluka kwake ngati a pa maliro a munthu opanda kwawo.
Chifukwa chakuti akugawa zinthu zaulere?