Email a copy of 'President Mutharika consoles Muluzi, Busile: JB sends condolence message' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'President Mutharika consoles Muluzi, Busile: JB sends condolence message' to a friend
Government of Malawi and the African Development Bank (ADB) Tuesday signed a loan agreement amounting to US$22.4(MK16.5Billion) to finance the...
R.I.P Nthawi zonse ndife maluwa. Ndipo sitimatha kuziteteza Allah adapeleka chisisi chomwe mwini kuzindikila ndi iye ife kuziteteza kwathu ndikulira. Ndikupempha makomo onse aku jaanah asegulidwe. Pamodzi ndi onse omwe atisiya munga abale ku chipembedzo. Mulungu Allah akuyikeni kuzanja lakumanja inshaallah manda anu akhale nulu yowala nthawi zonse Ameen
a Joyce Banda kundondela bwanji? Why only condole one family? Ndimayesa pali mabanja awiri amene ali a nnamfedwa. Stupid politicians thinking yawo ndi imeneyi. Anthu wamba like samawaona ngati kanthu. Iwowo is about pleasing fellow politicians. Amayi onamizila kupemphela amenewa. Mayi wamvano apepesa banja limodzi lokha when there are two bereaved families
Chindere, maybe the name befits you! Why blame Joyce Banda? Has the president also gone to condole the other bereaved family? When the tragedy happened, Nyasa Times also concentrated on the death of Muluzi’s daughter it was not mentioned that the other lady had also died although it was indicated that both had been struck by lightning. That is the way things are – If you are a nobody in life, your death too will not matter!
Pepani kwambiri
He wore a black tie. It doesn’t have to be a black suit.
its so sad and May their souls rest in eternal peace.
Pepani akumabanja onse awiri chifukwa cha zovuta zimenezi zomwe zatigwera, mulungu atithontoze tonse pamodzi ndi mabanja ofeledwa.
Rest in peace
Pumani bwino…kwathu si padziko ndingopitilira AMEN
Umati avale chiyani ndiwe foreigner wakuti ma be Tanzania ,kape
Petulo you are so stupid ngati chonena chinakusowa kuli bwino kukhala chete. Iyi ndi ngozi palibe amene anakonzekera ndipo izi sizandale ai. Kodi apa waonapo mbendela ya chipani? A president akonso palibe chimene anakunanepo ai ali pwii chonsencho ndi mbusa. Stupid kagwere uko, shatapu.
Zakhudza Chakwera why? unava kuti Petulo ndiwa Chakwera? ndikwanu komweko!!! ndi umbuli wobadwa nawowu mungatani? Leave Chakwera alone please!!!!!