Email a copy of 'Students at Teacher Training Colleges to start paying fees' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Students at Teacher Training Colleges to start paying fees' to a friend
The much awaited Malawi School Certificate of Education (MSCE) 2015 examination results are expected to be out in the coming...
Mmmmmmmmh Malawi ndiye waonongekeratu zafikapa eeeeeeeeeek kaya eti
Kwaaaacha! Kwacha
Mwaphunziraphunzira sukulu ndi makoleji aulere,muli pa ntchito zabwino,mukulandiranso ndalama zabwino pano mumvekere enawa azilipira,cholinga ana amphawi azilephera inu kukhosi mbee kuyera.Ena mukuti ku USA,munenenso minimum wage imene munthu amalai dira kumeneko
Not enough for cashgaters govt pickpocketers are hungry.
apa zafika pamwana wakana phala chala mwamba
Bad that
At the same time that students training to be teachers are told they will have to pay fees, Mutharika pledges that Malawi is to invest more in education. Contradiction or what?
DPP woyeee
Chala mwamba
Boma ilo.
Pa mawa muzawasankhenso akukuthirani motowo daily.
DPP woyeee
Chla mwamba
Boma ilo.
Pa mawa muzawasankhenso akukuthirani motowondaily.
Zovuta