Email a copy of 'Wanderers ready for intense derby with Bullets at Bingu Stadium: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Wanderers ready for intense derby with Bullets at Bingu Stadium: Malawi TNM Super League' to a friend
Silver Strikers who are losing track with their title campaign have appealed against the ruling by Football Association of Malawi...
Chonde Maule mukaluze mawa. Neba wanu asatuluke season opanda kolilira. Mupateseni Ligi atenge. Kumalemekezana ndinu akuluakulu nokhanokha.
manoma tikadya monona koma neba kugula ma ref game imeneyi akayimbira duncan lengani osati a china chizinga masapota a bullets ayi
NOMa akatundu enieni,Ulendo uno tikukamenya CAF kaya wina afune kaya asafune
Please inu a Nyasa, Be Forward komanso Silver tayambani mipikisano ya CAF kodi mumaopako chani???? ntchito ndikulimbana nokha nokha ife tatopa nanu shaaaaa!!!!!
Kkkkkkkk Neba Neba suzathekanso nthawi zones kudandaule basi. Pano wavomela game pa BIS kkkkkkkk