Email a copy of 'Win all remaining league games, Wanderers coach and players told' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Win all remaining league games, Wanderers coach and players told' to a friend
In my entry this week, readers please allow me first to express my sincere appreciation to all those who have...
goooo! Nyerere nebayu ndiwamisala we are the nomads timayenda ngati msomba
Ndkanena Kt Wna Alira Aayeee Alira di di di di Di Di Di Manoma Osachita Matha Waku Division Bas Shaaaaa Uzngodroowesa Bas Ndye Sponsorship Ija Ilipachiopsezo Kaya
Neba Nyanga Kufutha Nanga Lero Ndchan Chachitkachi Matama Thoo Bas Koma Kunyoza Azako Bas Uzngowna Azakowo Ati Angokhala Kumangokuyang’ana Ukuwina Kkkkkkkkkkkkkkk Ayaya Ngoleka Fc Uzona Chaka Chake Ndchino Kkkkkkkkkkkk
Kkkk
Wina akuti ndi internal matters so why bringing it out to the public?
BF is just an agent of car sales! sapanga ma motor. Ndamva kuti u hired an open van for cup parade! Since u lost the game then just parade your ng’angas for failing u. Nanga nokha ukalistiya while ena atapita kwa sangoma!
MAFCO ndiye iwonjezere chipsyinjo pa neba chifukwa lero ikupunthirani pakhomo,ife a Nyasa Bullets tizingosesa aliyense obwera mtsogolomu.
Ayaya akukwiira neba…………….. Ukamati uwina ma games onse ukuiwala zoti ukakumana ndi nyau zaku Lilongwe???? Inu kadzingozinamizani kuti ndinu olemera basi………………… B4WD ndi agent ogulitsa magalimoto chabe and ndi osauka……………… umboni muli nawo pa ASU plus kunyanyala kwa ma players anu aja………………. zoona kukanika kulipira rent timanyumba totchipa takwa a Goliyo tonseti…………… zangochitika kuti tinakubabada kale koma iwe umafunika kukupondanso……………. Mafco pilizi chonde atsotsombetseni ankhutukumvewa mosapsatira michira……………… Zabwino zones powina ma games onse. kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk ndakomoka
Neba kusamva…Neba ndinakuuza kuti osaphatikiza zinthu ziwiri.Pano ndiye sankha chimodzi.Nanga game ya Civo kugawana ena kupita ku Maula kukalandira ukalistia ena waku Salima kwa ujeni………Sintha khalidwe!!!
kkkkkkkkkk manoma more verbal fire as you touch your shaft ….koma kusowa zokanda hmm
If u r aiming of winning al the remaining games then u r at a beta position only if u hv improved ur striking forces otherwise the journey z nt yet over.