Email a copy of 'Witchcraft plane crash’ causes commotion in Kasungu' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Witchcraft plane crash’ causes commotion in Kasungu' to a friend
President Peter Mutharika is in the People’s Republic of China for a five-day visit that should unveil the next phase...
boma livomereze kuti ufiti uliko, ndipo lirole wochita zaufitizo kuti abwere poyera ndikutukula luso lawo lipite patsogolo kuti mmalo mwa ntcito zoipa azipanga ntchito zabwino. akhoza kuchita zazikulu zabwino zoposa.asaponderezedwe pokana kuti ufiti kulibe.ndegetu ndi transport.
ameneyo nde munthu wakuda
Ufiti uliko
Alomwe mumakatamba kwawo kwa kamuzu chamba eti
Amalawi kukhalila mankhwala, ma pailoti apita kuti andegeyo.
Did you expect an Airbus A380 to fall on this house? Witchcraft exist because this is a way that the devil manipulate into sin most of the poor and backward minds of the world. Others are saying kuti ndi chidole, can a normal person make such a hideous and awful craft for a kid to play with? He will run away at its sight. Witchcraft exists the world over: in the Americas, Asia, Europe, Australia, Oceania and its real hub Africa. Don’t’ be deceived that kwa azungu kulibe ufiti. Ufiti ulipo ndithu kumeneko that is why he came up with… Read more »
So how many people have died?It seems they didn’t get permission when they were flying over the air space of the owner of the house.Tell Mr Nthidwa of humanist organisation to collect it and put it in his office.
Ife takhala tikukwera zimenezi kwa nthawi koma ana a masiku ano matama, kuuluka po tsilika ndi izo mwakhaula nazo. Kupusa kwambiri
OK GUYS, WHO HAS EVER MET A MEMBER OF THE DRUID FROM USA? SMALL MINDS DONT BELIEVE IN UFITI COZ OF LACK OF EXPOSURE.
Amalawi sitizatuķukapo mkamadalira zitsamba, inu simuķuona ķuti chimene mwatengacho ndi chidole ana ama seweĺetsa kenako kuchiyiwala inu basi kumati ndi ufiti apolice nanuso ndinu mbuli zo mphunzira.