Email a copy of 'Kanyama new IG Malawi Police : Dzonzi heading to UN' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Kanyama new IG Malawi Police : Dzonzi heading to UN' to a friend
Published report on Saturday November 22 indicated that First Lady Gertrude Mutharika’s Beautify Malawi (Beam) Trust and tribal grouping Mulhako...
NEW IG WABWELA NDIKUPHA, JUST 2 DAYS KUKHALA PA MPANDO, ANYAMATA AKE KUPHA MUNTHU WOSALAKWA NDIYE KUTI WAWUZA APOLICE AKE KUTI ASAWUMILE KUPHA ANTHU, MMANJA MWANU MULI MWAYAMBA NDI MAGAZI BWANA SHAME, RIP SOLDIER MILANDU KWA MULUNGU ILI NDI MABWANAWA
IG ONYASA NKHOPE…..EYA MSILIKALI AZITERO….AZIKHALA OKWIYA ONYASA NKHOPE CHONCHI…..GONGRANTS IG….
wa Police amakhala woyela? NANGA JOSE AKUTANI PA DEPUTY IG? IWE APM, WHAT ARE YOU REWARDING JOSE FOR . ARE YOU ACCEPTING RESPONSIBILITY PA ZOMWE ZINANCHITKILA MWANA UJA?
Congratulations to the new IG and his Deputy!Mizimu ya ma Teachers athu pa Kachere/Ndirande primary school ya vomera kuti ‘Yes’ anyamata tengani maudindo! I am proud of you guys,Rodrick and Rodney!Ndirande ‘Ooyeh!
Malawi World War 1 Yayamba mu ulamuliro wa nyapaphi.
God bless you Lot Dzonzi. You restored the good relationship between the police and the civillians which was broken during Bingu’s error. You are a proffesional, a believer and a servant of the people. We hope you will even evangelize the UN.
Dzonzi wachita bwino ukapume asiye aziphana agaluwa ndi nkulu wao iwe ndi opemphera
Training ya 6 months amafuna azilandira K100,000.00?
HONEYMOON IS OVER IG SAID ——- ONLY AFTER TWO DAYS MDF SOLDER HAS BEEN KILLED ——— OSUNGISA BATA OKHA-OKHA KILLING ONE ANOTHER WHAT IS THAT NOW. NEW IG YOU HAVE STARTED WITH FULL BLOOD OF A SOLDER –VERY SAD OF YOU IG. SORRY MDF.
Nayenso msilikali amachokera kokuba. Waiona shoot to kill. 11:00 pm? amachoka kuti?
Kanyimbi u are right. Asilikali pa Cobbe amadzimva kwabasi. Amachokela kuti, ndipo mPolice anali pa ntchito yake zinazi kumamvetsetsa.
Apart from buying them cars, improve the welfare of junior police officers. Salary yawo ndiyomvesa chisoni