hhehe ikakhala nkhani yoipa nde olemba nkhani saziyika dzina..koma ikakhal wine house treats its guests nde dzina apooo…oh yes Malawi wathu uyu tizidya tonse basi
nana phiri
9 years ago
zakumanyazi basi,,osangotenga ma blaks bwanji,,Davido nde kuti vichi?
Mangoria
9 years ago
Thats good. We are mourning anzathu apita ndi madzi ena katundu wawo wawonongeka. Mwachita bwino
hhehe ikakhala nkhani yoipa nde olemba nkhani saziyika dzina..koma ikakhal wine house treats its guests nde dzina apooo…oh yes Malawi wathu uyu tizidya tonse basi
zakumanyazi basi,,osangotenga ma blaks bwanji,,Davido nde kuti vichi?
Thats good. We are mourning anzathu apita ndi madzi ena katundu wawo wawonongeka. Mwachita bwino
zofuna!ulesi basi kungofuna zolandira chaka chilichonse?stupid
basi tagotengani chibade ndi joy gwaladi kod amalawi kukhomelerana tokha tokha adzilemera obwera basi?
Or Davido is who?
kkkk…just host anthu anthu akunowa…abwera mamawa omwe
He is afraid of NACGATE mastermined by First Lady and her husband Peter
Akuopa NACGATE masterminded by First Lady and her husband Peter
mumangot davido davido mose muja anayambira kunama muja. amalawi simudzakozekadi bwanji osangomutenga lulu. mxiew
mbuzi chitsiru moti azikalimbana ndi book haram