Email a copy of 'Thyolo prostitute arrested for murder: Allegedly killed man who failed to payfor sex service' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Thyolo prostitute arrested for murder: Allegedly killed man who failed to payfor sex service' to a friend
Malawi national football team regroups on Tuesday in preparation for the Africa Cup of Nations qualifier against Zimbabwe on June 13 at Kamuzu...
Mphoto yake yauchimo ndi IMFA kuti udziwike kuti ndi uchimo wamubalira imfa mbaleyu pepani. Tikazipata ndalama tiyeni tisamale
T hpenz
Akweni ndipofuna kulowelerapo apa.Abambo achilomwe a gondolosi akuchitidwa nkhaza ndi azimayi oyendaoyenda Ku Thyolo.You are so quiet on this issue Madam Kaliati.Why are you gender biased?
Uku nkupusa uku hule kukutsegulira Iwe kumabweleranso umafuna ukamenyenso INA munthu ulibe ndalama.kapumeni bwino ife tikanathana nawo.
Mahule tsopano!
Aminister madam Kaliati act on this to show gender equality.Dont be bias Mama,what goes around comez around.
Mmmmm amabungwe mutipo chan ife tingot pheee tioneeeee
kumawalipira mahulewo mukawanyenga, azikagula soap ndi mafuta ozola, kumalo kujatu kumafunika kuti azisukakonso
Kkkkkk Koma Abale Pofera Salambuladi Eeeee Ndamvetsetsa
izi ndi nkhaza kwa abambo.mesa analanda kale shoes, mrs p kaliati paja mumayankhula kwambili zikakhala kwa amayi,apa tayankhulani timve.