Email a copy of 'Up up goes beer, soft drink prices in Malawi' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Up up goes beer, soft drink prices in Malawi' to a friend
Malawi Police have arrested another man posing as a doctor was arrested at the country’s major referral centre, Queen Elizabeth...
Ife tisosolabe bawa ngakhale mukweze mowa. Paulo lero ndikhala mlendo wako. Koma pano mowa tiziyendera mawu oti “old trafford” meaning aliyense azigula wake
timwabe.zogulirana zatha.aliyense azigula wake enanu kususuka.
Izi nde zachamba. U jus knw how 2 steal our revenues then hike the prices of stuff entertains us!!! When’ll Malawi get unscrupulous leaderz who knws how to improve the livelihoods of its pple. Omwa bawa chaka chino ndi nzungu guyz! ! ! !
This will mean more time at home = baby boom shaaaa!!! nde population ifika pati coz pipo will console themselves with mdyingido.
Nayo Masm akweza . Malawians this is time to act. Go to the streets and remove these votes thieves. Boma lakuba ndichocho you do not know how to handle things. If one failed to handle a ministry how could he be entrusted with the whole country. Shame.
I fear more liver chirrhosis.Hike the prices kill the ppo.Bagi ndi kachasu tinthananazo.Izo nzanunso.
MY WIFE ,THANKYOU 4 DE TOBWA INTHE COOLER-VERY NUTRI.
WHERE IS MALAWI HEADING ?ZIMBABWE STYLE LETS USE DOLLARS /MALAWI KWACHA IS SHIT/LETS PROMOTE OUR CHIBUKU THAN GREEN ETC
timkanena pitala uyu palibe chomwe anachitapo atchivi pamoyo wake kupatula kukwatila atangobele mavoti. am;boma walepheraso kukweza malipiro koma msonkho womwe akwaza uja wadula meaning the net has gone down. amalawi ngati tilekerela izi tivutika chifukwa chilichonse chakwera. its either masss demonstration or fedualisim by xmass
The number of people dying from satchets will increase in Malawi.If people cud hardly afford beers from previous prices.I don’t know if bottle stores r ever going to make money.Ndalama za cashgate amaseweletsa mumakomboni umu ndi izi azimayi akumayendera kumakaperekela nsima Ku Maula.Kwasala tizingomwa thobwano akugulitsa mumakhonde umu.Fanta tizimuonela Ku chikwati ndi kuchipatala basi.Koma moyo wafunga pachilawizi.Wolumikiza green pa bottlestore ndi mwamuna.Palibenso zogulirana mowa pano.Ambiri pano athera Ku ma satchets.
Green,stout & special @ K400? ok tizingomwa special yo apa basi.