Email a copy of 'Wanderers unbeaten run ends with Silver defeat: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Wanderers unbeaten run ends with Silver defeat: Malawi TNM Super League' to a friend
Dedza Young Soccer on Sunday secured a valuable three points after seeing off over Kamuzu Barracks at Dedza Stadium when...
We alws stluggle in 1st round mabanker ndi mabanker basi.
SILVER MORE FIRE MWAKHWANA MA BANKERS MWADYA MONONA.
Silver ni power wapapi Chaka chino chikho titenga basi.
kaya munyoze maule kuti akapolo dzulo mwaluzabe inu akanyimbi,agologolo ,akhakhakha,agulugunyida nsabwe zili thoooooooooooooooooooooo.mxiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii nyerere zonse zakhunyu!!!!!!!!!!
Backward wanderers ziliko chakachino koma Silver inakukwatirani bwanji mpaka ka 7 mondondozana kukuchinyani?.Ma Noma phokoso lokha mpira siitha! koma muisova chaka chake sichino, sibasi mwayambapo kuluza, mpaka Eliah Kananji posachedwapa mumuthamangitsa paja simuchedwa a lithumbu inu.Tizamvanso Kananji ndi wa Bullets koma chonsecho mumadziwa kuti ndi Maule oye!!Tili nanu pa 27 pano muzaona chomwe chinatchulitsa Bullets kuti ndi ma Palestina.
Ndakumvetsa, ukuti game isadzaseweredwe pot maule awina kale. REMEMBER THAT NYERERE zimamenya zokha nkhondo,MDZAFA IMFA YOWAWA ma hu le nonse
Nyerere ndi nyerere basi osataya mtima next game zidzayenda bola kulimbikila ,kuluza ndi silver ndi tsoka kwa bullets isamale loweruka lino IFA imfa yowawa kwambiri. Noma chaka chino ndi mofire kuwina basi kuti wawawa.
Namalira samutapa nkamwa. Ndaonera wina apa chichewa chake ngati chakutchire.
imene ija inali training chabe kukhozekera mahullewo
inu a Bullets nonse ndinu akapolo anthu osaphuzira abulutu inu simukuziwa chomwe muchita ndichomwe chikubwera agalu antchile achule inu muziona pa 27
Mukhalira ma hiii!! hoo!! MUSOVA!!! Ather wise ths coming weekend muliraso mokwexa hahaha MAULE WOYEEEE!!!!..