Bullets seal title, beat Epac: Malawi TNM Super League
To any doubters on Big Bullets retaining the TNM Super League title, they have been answered that the Bullets are going all the way to be crowned champions back-to-back after they opened a 13-point gap between them and second placed Mafco on Saturday.

Bullet defeated Epac FC at Civo Stadium in Lilongwe and condemned them to relegation danger.
The champions won on Chiukepo Msowoya’s 29th minute goal after he rose high to head in a well-curved Yamikani Fodya set piece past a helpless Epac goalkeeper Tione Tembo.
“We are waiting to be officially crowned champions. But as you can see, we have sealed it. It’s in our bag,” said Bullets team manager Rahim Ishmael.
Meanwhile, Epac coach Abbas Makawa said he has big task to pull off his side form relegation \one as they are sitting second from the bottom of the log table.
Mr Chiukepo you flopped at Pirates in RSA, given a platform to shine but alas, nothing total failure ndiye pano pomati akuti a Dolo ku Mpanje shame.
Neba ukamamva The Peoples Team ndi imeneyo, osamangosapota zilizonse, many years without sponsor tokha masapota koma chilichonse ndikumatheka ndiye pano ndikubwera kwa Nyasa, mumva kuwawa nonse, chaka chamawa tikutenganso paja tikumatengeratu 1st round unbeaten record waziziwa? Ka Airborne mumakatama kaja kakukasewera Chipiku pamodzi ndi Kasungu Medicals koma ziliko liko wina akomoka chaka chake ndichino maka ma cup specialist wobokiratu AXA Shuttle
A neba mukuti bwa? Mwawawona Mawuuuuleeeeeee? Ngati tatenga championship kawiri opanda ndalama, ndiye panopa mugwirana nafe? Mabwana aku Be Forward mukumva bwanji? Si zamanyazi izi? Zaka zikubwerazitu mutimva kuwawa ndithu, chifukwa apapa ndiye sitidziyang’ananso kuti pali ndani. Kaya ndi a neba, tidzingokutumula kwinaku titatseka mmakutu kuti tisamve kulira kuopa kuti tingamve chisoni. MORE FIRE BULLEEEEETS!
zotheka maule
wina afune asafune BB will remain champions in Malawi.BB woyeeee!
Chitimu koma chimenechi maule moto kuti buuuu!!!!
Ukakhala mu mtsuko wa mkaka sumwa matsukwa BB ndi more fire!kkkk.
Mutimvanso kuwawa next season maka tapezano otithandiza nduye eeee
That is my team. I am 46 and i support my father’s team. Anandisakhira boo!!!! Mapalestina woyeeeeeee.
After so many dry years of not winning titles, now titles are won back to back
Wonyamilanduyo anyazipwisi.
Bullets to be crowned the champion of malawi soccer (Nyasa Big Bullets)usokonezenso wauze anyasawo kuti atengonso manoma
Ndilibe nayo mau BB, ulendo ulendo ulendo wa ku caf
“Ndati zinthu zitani heheheheeee kuchitekete” “amai nda bambo ngati anthu amayesa kuti ndine mphaka, ndine tiger ndkukandakandani” “zinthu zataani……? “Kumpoto! Bullets!!! Pakati Big!!! Nanga kummwera! Nyasaaaaaaaaaaaa! Dziko lonse! Nyasa Big Bullets!!!!! Neba, neba, neba! Wake up, you are a big boy. Stand up! Stand up! For the champion, for the champion. Keeep it boys, you are the one puting a smile on our face.
Maule more fireeeeeeeeeeeeee,,,,mpaka wina alire basi
what a golden team!viva chiukepo,fodya,nyasa manufacturers, terminator,etc,
That’s the pipos team I know!!!!!!
It all started with us beating the bankers and nomads who else is there to stop BB from grabbing it…Teams can only delay BB but not stopping it from being crowned champions
Is it true Mphwiyo is out on bail???
If true the judge must humbly resign or like minded people are going to mobilise to take the law into their own hands.
STANDUP 4 THE CHAMPIONS. BULLETS WOYEEEEEEE ,NOW START TRAINING TO GET READY 4THE CAF HAHAHAHAHA
Why using std bank picture? malawi @ 50
Kuwina koma kumeneko osati zomachita kubelekedwa ndi ma ref kkkkkkkkkk koma neba ukuyenera kupita ku chipiku basi ukasewere ndi ana anzako koma oberekedwa ndi ma ref palibe chimene chingakuthandize look NYASA BULLETS KKKKKK IFE ALWAYS CREAMS OF MILK ON VE TABLE shame on u neba!!!!
MAULE OMWEWO KUT WAWAWAAA ! MPAKA TITENGA MATRIP 10 ‘SUPER LEAGUE’ KUKUMBUKIRA MATRIP 7 A PA ZANA PAJA.
Chaka chinonso Maule atenga TNM Super League. Amwedwe basi wa mkaka! Neba ukumva bwanji mu mtimamo? Ha ha ha!
Maule woyee… Chiukepo now work hard for the golden boot.
THATS A NICE ONE. WE ARE ALMOST THERE. CONGGRATS MAULE.
Koma paja Neba amati alimbikila kwambili kuti atilande, kaya, tiziona paja Neba ali ndi njira zambiri like buying ref e.t.c .Alibenso manyazi poyankhula amakhulupilira zosatheka kkkkkkkk mwina zitheka dzana sanali pa No. 10 kkkkk.WOZA MAULE !!apwetekeni ana osawanyengerera ngachipongwi kkkkkkkkkkk
Thats nyasa big bullets which i know.go on maulee!!!!!, we r de champions of tnm super L without any doubt.wth u chiukepo top goal scorer&fodya de player of de czon.
NTCHITO ZA MAPAZI AWO ZAWACHITIRA UMBONI, APATSEN BASI.
Pincode ya league tili nayo tokha…Nyasa Bullets woye!
Maule sakunyengelera,koma akuchita zantchito basi wamva neba.
Congrats maule
woza maule ,keep on fire burning. neba agwire chipwisi, njenjete no longer our agemate.