Email a copy of 'Activist Simsokwe joins frontline politics: Chakwera welcomes ‘new blood’ in MCP' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Activist Simsokwe joins frontline politics: Chakwera welcomes ‘new blood’ in MCP' to a friend
Central Region based side Civil Sporting F.C and Northern Region giants Moyale Barracks are through to the round of 16...
Mbava za dpp zichoke. Dpp yatsango. If you’re not Lomwe yenda zako shamwali.
Chipani chikununkhila,,,,,,,Chakwera 2019 bomaaaaa!!!!!!
Most welcome bwana chipani cha
fuko la Malawi
Cadet wapsa mtima.
Chitungwi bwanji ma cadets kumeneko, simutsekula mmimba chaka chino.
Yeah, otsatira kulowa MCP ndi Mtambo, kenako Kajoloweka ndi Trepance.
Rights reserved
Let’s wait and see
You would have been happy if he joined dpp. You would have made a lot of noise. Leave him alone . He has freedom of association. There is nothing in Dpp that people could join for. Only kuba ndalama za a Malawi. Ukagwere uko.
Kodi osakachita report anthu amene akukuberani ndalama zanuzo ku police bwanji ngati muli ndi umboni? Monse munayambira akutibera ndalama akutibera ndalama koma palibe chomwe mwachitapo report, olo kumva kuti chakwera watenga ma file uchitira umboni kuti wakuti wakuti akuba ndalama, wapita nazo ku police? siyani kulira nkhani yoberedwayi tatopa nayo. Inu mwachita kutani kuti nokha nokha mukaberedwe mavoti ndi ndalama? Inetu apa ndimangophera mphongo malinga ndi nkhani yalembedwa apayi, kuchitira umboni kuti ma activist ambiri ndi ma ambassador a MCP.
Carrying the same pains with majority of Malawians, I like what you have said in chichewa kuphera mphongo, you are such good boy,.
Pathfinder uli mmalawi mommuno koma? Zoti ndalama zathu za misonkho zakhala zikubedwa sukudziwa? Ndiye uli mtulotu, wafunda bulangeti la joni kkkkkkk. Dzuka Malawi dzuka!!!!!!! MCP bomaaaaa
A TAMALISHA mukuona ngati akutibera ndi campaign tool? Wokuba amachitidwa report ku police. Rural people can’t take that bullshit seriously. Zomwe akuona ndi chitukuko. Indeed, prepare for atibera vol 6. By the way, MCP is not national. Ever heard of MEC complaining that these so called opposition parties are failing even to supply monitors country wide? Akakhala awa a moto wa mapesiwa ndiye kungothandiza a mfumu kuledzera. The way opposition is bahaving is like a team that is always defending and not attacking. Ati kuonetsetsa kuti ena asadzabere yet no substance to the electorate while the DPP is digging deeper… Read more »