Email a copy of 'Cops assaulted in Mzuzu: Malawi Police plays down incident' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Cops assaulted in Mzuzu: Malawi Police plays down incident' to a friend
Malawi national soccer team the Flames has moved 15 places up the ladder—from 109 to 94—to find their way back...
Njovu zikamamenyana umatikitika ndi udzu. osakangana ndife ana kamodzi
ine dothi ndatapa kale…akufuna aphume tiwonerepo ndewu ya makape amene salemekeza ufulu wa ma civilians
Vuto ndilakuti wankulu wa polisi malaya ake zingwinjiri zokhazokhs naye waMDF zingwinjiri zokha zokha sopano wankulu ndi ndani apa mumadererana .
Choipa sabwezera
Bongololo – 22.1 – R U a believer or not? Can’t u c that our God has alreaday intervened. Peace will prevail in Malawi whether one likes it or not. JESUS IS LORD!!!
Eish,pakhola apa alinamwana agwiritse
Kaning’ina simacheza thats lesson number one
SHEE moyale sopano anyamata aku nchenga utuwa kuzolozolo, eish mwati sama omberekakunfuti kumangotuluka madzi kuti fwaaaa.
Come on Mr Chapola, don’t say its normal, say it happens. And when citizens are frequently victimized by crime then its security lapse….but when those who are responsible for maintaining order are victims thats even worse than just security lapse.
investigation on s death and incuddnt with names & time date u.mfiti eti mumajafynz
se kumandako? nduts amakyzani ndani mizimu mpK amakyzinilNi report ir sratement ziha makalemba mchizungu cga venecular.
dont tell me u want ti know his/her blood group or shoe size…oops paja mafuna mtubdu what value does that add ti a case? ndine mmalawi ivadwira ku mvera does not mean am ngoni or chewa! please lets get rid of this thinking zats why timayiqala qhich are the core ethnu groups ib mlw…but if we persue these its discrimiinatory practice it must stop….
Walemba zosamveka koma muli tinzeru pang’ono. Can you be clear with your writing plz