Email a copy of 'Dad who deserted 11 children for new wife arrested, says Malawi Police' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

32 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
ZAKUNSI
ZAKUNSI
9 years ago

Mtumbuka iwe ana onsewo umati ndi achiyani? Umati ukadya kapena ukagulitsa? Iwe akunjate ndithu.

Ronnex
9 years ago

Akamumanga ana adya chan?he just hav to b gven a punishment of oeeding the forbiden children

Dobadoba
Dobadoba
9 years ago

Apa ndiye a Court/Police amasuleni bambowa chifukwa anawa avutika kwambiri komanso agogo awo akhala m’mavuto kwambiri. Malinga ndi mwambo wachitumbuka wamalowolo ana amakhala ndimwamuna zikasokonekera. Nchifukwa chake mayiyo anachoka yekha kumapita komwe aliko. Ana amenewa ali kwa amayi awo a bambo awo.
Chofunika nkukhala pansi ndi bambowa kuwalangiza bwinobwino komanso kufufuza komwe mayi wa anawa ali chifukwa anawa ndi ambiri ofunika bambo ndi mayi awo kuwalelera pamodzi kuti akule bwino. Apa a Police/Court gwirani ntchito yanu bwinobwino muwathandize anthuwa mwaukadaulo wanu. Amasuleni ndithu bambowa.

meya
meya
9 years ago

Mwachita bwino. Koma zimenezi zizionedwa bwinobwino. Coz ana ambiri anayamba uhule, kuba etc chifukwa cha zinthu ngati zimenezi. ambiri atengerapo phunziro. Makamaka mmamidzimu entertainment yao ndi sex basi ndiye ananso amachuluka nkumasowa kuwasamala kwake. Bamboyu ndiwankhanza anao amuchulukira nanga kwa mkazi winayo safunanso kumubelekera. kp it up. For future generation.

Kwame
Kwame
9 years ago

Munkhanimu Amayiwa akuti anachoka chifukwa mabvuto a za mbanja nde kuti bambowa ndi ozunza. Ku mpoto ana ndi abambo chifukwa cha mwambo olowola nde mukakhala mavuto mubanja mkazi amamusiyila mwamuna ana kuti aziwasamala chifukwa mkazi amakakhala kwa mwamuna osati mwamuna kupita kukakhala chikamwini. Apa mwamuna amayeneleka kusova mavuto a mubanjamo kuti onse azisamalira limodzi ana. Mkazi anali pa mabvuto ndi abambowo anatopa nawo mabvutowo. Amamupanikiza kwambiri mkazi pomabeleka ana pafupi pafupi. Taganizani ana 11 nde mkaziyo amawopa kubeleka wa 12. Nde kuti bambowo amamukaniza mayiyo njira zolela nde mkazi anangoti ee pachepa malo ndingochoka kumusiyila anawo nanga si bambo ndi… Read more »

Kwame
Kwame
9 years ago

Iwe Ammatuwa za ugalu zomwe walembazi. If u hav nothing in your brain to say just shut up your big and ugly mouth. Si zonenana mitundu apa. Atumbuka ndi alomwe atani. Iwe mtundu wako ndi chiyani? Tinene kuti mchewa? Zopusa zimenezi. Zimatengela mtima wa munthu nyani iwe. Xenophia ku malawi kwathu konkuno. Ndiwe nkhumba yoyenda maso akuyang’ana pansi. Kodi a nyasa muziona ma coments owasiya pamenepa. Ma coments ofuna kugawanisa mtundu muziwachosa.

aheli moto
aheli moto
9 years ago

thats very good , koma mutabwera u South nde ma cell azachepatu because most men there are so heartless with their children. makamaka in impoverished homes. amngonyamula bulangete lawo wautali kusiya ana kwa mkazi iwo kukalowa banja kwina

za manyazi azibambo otere

Emmatuwa
Emmatuwa
9 years ago

Nyere atumbuka simunasiyane ndi Alomwe

khokhola
khokhola
9 years ago

Where is the mother here? Arrest her too. Who said the father alone shall be responsible for looking after the children? Do we have such law in Malawi? Just discuss with the employer of this man to deduct half the salary every month and remit the same to the grandparent for feeding the children. If you force this man to reunite with his children , expect death of either the man himself or the daughter who reported to police. This man is bitter. Why did the wife run away? Remember, people hang themselves once they realize that they are useless… Read more »

kangandiwamba
9 years ago

kkkk

Read previous post:
Prison boss charged with murder after shooting sons

Deputy senior station officer in charge of Chichiri Prison senior superintendent Evance Kataira Chisi has been charged with the murder ...

Close