Email a copy of 'DPP, UDF supporters clash, defy Muluzi and Nankhumwa unity call - Report' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

20 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Frankly speaking
8 years ago

Kodi ku Esatern region simumatha kulemba mu Chizungu? This is an English online media – you can write in English ? kumeneku sukulu idasaliradi eeishi !

Cheidana
Cheidana
8 years ago

Ife a UDF ngati titapeze mavuto ndi chifukwa cha dyera la Atupele ndi bambo ake. Inu nomwe munatipitisa ku PP amai Joyce Banda atangotenga udindo wa president, mwakawona zoti mimba zanu sizikunkhuta mokwanira munatiwuza kuti basi tipange za agenda for change and ife tinavomeleza. Lero mwati ayi koma ku DPP mwayiwala zoti ndinu nomwe amene mumatituma kukawotcha mmisewu ku Mangochi kuti Peter sanawine. Lero mukufuna kutizunguzapo mitu ndi dyera lanu lake mgwilizano kanu kopanda sogolo ka. Ndiye mawa muzizati tiyeninso tipange za UDF. Ayi ndithu bola kusiya ku sapota UDF yi sopano. Tisanamizane DPP pano ikumeleratu mizu ku chimbundiko ndipo… Read more »

ibrahim makwati
ibrahim makwati
8 years ago

ili ndi chenjezo kwa atupele ndi onse okonda kumango vomeleza zilizonse chifukwa chokonda ndalama samalani muzasala nokha popanda okusatilani

Dwambazi
Dwambazi
8 years ago

Njoka saweta

Moya weniweni
Moya weniweni
8 years ago

Palibe zomuyipisa governor wa DPP ku Mangochi ko ayi. Ife ngati a DPP ngati chipani cholamula mumafuna kuti governor wathu akhale pansi ndi atidye nawo a UDF? Never ndipo ife sitilolera zopusazo palibe ubale pakati pa UDF ndi DPP coz njoka saweta. Chisankho changothachi bwanji a UDF amamenya ma sapota a DPP ku Mangochi kwanuko ngati DPP imapikisana nawo. Please our dear president beware of these UDF as they are planning to overthrow your government as a revenge of Bingu’s dumping of UDF in 2005! Even without these UDF pipo DPP will win with landslide including some MPs in Mangochi.… Read more »

Dr Mbewe
Dr Mbewe
8 years ago

Dpp and udf all thieves they belong to prison

chandamale
chandamale
8 years ago

Its indeed eastern region always with problemswhy is it so the leadership has alot of problems specially bwana RG wa DPP amalephera kudzuzula District governer wawoyo kaya umphawi i dont know be civiliazed people anthu anagwiliza onkha inu ndi ndani kuchipani komanso SG i mean Mr kudomtoni bwanji kulekelera zotezi komatu mumvi oyang’nira ok

tsetsefly
tsetsefly
8 years ago

I can see UDF well wishers have sensed danger in this marriage of convenience. They don’t want this panga knife party to swallow them in broad day light. UDF is suffering from leadership problems because Atupele is a young man full of greed and has demonstrated to be the worst youth leader. I think he rides on his dad’s back otherwise he could not have been the party president. Unfortunately for Malawi parties have become family properties and as such parties are more of liabilities to Malawians than assets.

chatonda
chatonda
8 years ago

this is the end of Atupere’s political carrer just like Aford and Chihana did. He is an opportunist and he only wants to be a minister despite the party loving UDF as a party on its own. He is following his father’s political carrer of roping others for money like he did with Gwanda and Chihana both died poor of course. He too will die poor. He cannot take his supporters for granted and assuem they agree with his political prostitution habit. Somebody will rise up in UDF nad form his own team totake the UDF leadership. He will regret… Read more »

MAMUNA
MAMUNA
8 years ago

ZONSEZI NDI CJIFUKWA CHA ATUPELE KUKONDA MAUDINDO NDI CHUMA

KOPOSA IFE WANTHU A KWAWO

Read previous post:
In the whiff of DPP rule: Malawi situation, we are certainly in this together

The DPP government is fast cruising to a destination. I would have loved to name the destination but I am...

Close