Email a copy of 'Ex-MP for Machinga-Likwenu endorses Msaka’s candidacy' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Ex-MP for Machinga-Likwenu endorses Msaka’s candidacy' to a friend
Local Government and Rural Development Minister, Kondwani Nankhumwa has laid a foundation stone for the construction of a school block...
Sachebetu apa, ndikuganiza kutii mayiwa agudwa.
iya amayi mwakhuta a jangiya eti musawauze anthu chokavotera anthu aku machinga ndiwosukusula avotera mcp osati a bright msaka wo ayi inu kapumeni musatikwane amayi opanda chitukuko ngati inu sindinakuoneni ndipamene mwa surrender kusonyeza kulephera pitani mukapange za banja
paja he is a running mate eti mwana wa bakili ali mmadzi ayenda tibiya tibiya mpedzi pedzi
Jangiya, you knew very well you could not fight Msaka. And you remembered an adage that goes ” if you can fight them join them” Who does not want to be a MP especially when you were one before? Msaka could be a strong man but he is entering an electoral race riding a dead horse (DPP). We know he will not win. His party is riddled with poor performance, corruption, abuse of public offices and nepotism. These are his key obstacles to success. People of the constituency are aware that meaningful and sustained development cant take place in corrupt… Read more »
Anthu ophunzira bwino sukulu koma kuzerezeka ndi ndale zakuMalawi zokhalira kubera anthu. A Msaka akuti sapolomisa anthu kalikose komahso akuwuza anthu kuti sazafa ndinjala.
Supota weni samasunthasuntha or team yake iziluza life ndi a UDF basi no matter what