Email a copy of 'Kulemeka Mothers Day bash showcases K7m Ngoni attire' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Kulemeka Mothers Day bash showcases K7m Ngoni attire' to a friend
Leading mobile telecommunications provider Airtel Malawi has launched the Distributor Engagement competition that will recognize top three performing distributors from...
Two of the ladies are anya singini aka mrs Ghambi the hubby used to wk for malawi army he was a pilot
zanu izo ife nde tinanjoya…. keep it up next time tili konko. The invite just said ngoni attire aliyense amavala zachingoni according to her….Nsanje amalawi tapanganitu ma bash a culture yanu tione!!!! mimbazo ndi zathu, ndalamazo zathu vuto lacho nchani ada!!!
So fat and ugly. Malawi must have some of the ugliest people in the world!
modern ngoni attire. kale izi kunalibe
Azimayi munatchena ! tasilira enafe tinali kutali, next year moto moto! asafuna asamuke!
Winawe ndiye ukufuna uoneke odziwa lero za zobvala za chingoni, za Amalawi? Ati Ngwazi, chani chani……….mwasowa chochita. poti mayi kulemeka wayambitsa? Unali kuti nthawi yonseyi?? Tamakangodyani matewera ngati mwasowa chochita.
Mwasilira AMalawi, (akaidi) mukuti inu mukudziwa attire ya chingoni, ya chi Malawi, ndiye kuti chani? Ndimayesa Angoni akumalawi anachokera ku South Africa? Nsanje idzakupengetsani nanunso inu!!
Enawo ali deformed ndi ma ARV’eti nanga khosilo? The lady third from left and the last on the right ayayayayayaya. Pepani. Plan for lipo…….it works
Kusowa zochita.
Za ziii!! Vambula salt.This is south African attire not Malawian,show our attire ie Malawian.Nthawi zina tizikhala ndi nzeru popanga zinthu.Am angoni but I will not support this nonsenses called ngoni attire I never known this as our attire sa attire.