Email a copy of 'Malawi new Accountant General hired: Chrighton Chimombo' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi new Accountant General hired: Chrighton Chimombo' to a friend
Kamuzu Barracks Volleyball Team are the champions of the 2017 Raiply Volleyball Tournament in the men’s category while Moyale Barracks...
Ku ACB kwapita Mulomwe winanso ……
Si mulomwe wina uyu? paja dpp
takulandilani abwana chimombo accountant general koma choyamba muone ma regional treasury cashiers makamaka southern region region treasury cashier musinthe utsogoleri wapa menepo because ntchito ikuwakanika a regional Treasury cashier mrs janet s phiri ma cheque akuchedwa kutuluka ntchito yaima ife ama cost centres tikudandaula kwambiri komanso uyu mati edith tandwe accountant mumchotsepo akuonononga ndalama za pension administration kwambiri mubweretse mnzibambo asinthe ma poor services because panopo zinthu sizili bwino ayi.