Email a copy of 'Malawi Police rescure two criminals from mob justice, arrested for impersonating cops' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi Police rescure two criminals from mob justice, arrested for impersonating cops' to a friend
Law Society of Malawi officials have described as not credible and independent the appointment of a commission of inquiry into...
Get rich or die
i hate thieves
where can I get such uniform? I need 1 for me, and 1 for my wife…..tizivala popita ku church
Nenaninso kuti anavala police uniforms!! Mukubisa chani apa!!
Akalandile chilango chokhwima kwambiri kupangira ena adzatengerepo phunziro. Kuipitsa dzina la munthu kapena ntchito ya wina ndi chinthu choipa kwambiri chifukwa anthu amaganiza kuti wachita zinthuzo ndi amene akufalitsilidwa dzina lakelo. Pano ndikunena za a Police omwe amanyozedwa mwa njira zambiri kuti akupanga zotsayenera pomwe asali iwo mmene zilili panozi.
O………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………………….O Let each one of us do some soul-searching; and honestly answer this question [within him/herself]. . . . If someone was to borrow or steal our face or identity and wear it, what is the first or main thing this person will do or occupy him/herself with [wearing our face]? Kodi azilanda akazi/amuna aeni easily? Kodi azilandira ziphuphu? Or do some bad or good stuff? . . . You see, “A friend is a good mirror.” We can therefore safely generalise and conclude that whatever this person would do with this stolen identity, is exactly what the owner of… Read more »
koma mamembawa ndiye akudzulidwa. apanidwe matopuwa awatenga kuti?
Where did they get the uniforms they are putting on? God forbid-they are lucky to be alive with the grass blanket that is ready for inferno + hell.
Dollar yavuta basi.
Alape