Email a copy of 'Mcheka Chilenje, Chizuzu in DPP fierce battle over Nsanje north: Nankhumwa diffuses tension' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

8 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Chameleonesentimentals
Chameleonesentimentals
5 years ago

Pathfinder, follow the issues correctly. Akuti Kaliati ndi andzake anakana bill ali ku DPP ACB koma panopa akuyifuna ali ku UTM Buses. Ulibe nzeru wamva. Usamangoyankhira wamva

che nnungu
5 years ago

Chala mmwamba but the faces look gloomy

mandala
mandala
5 years ago

The faces i see in these pictures looks very poor and malnourished i feel pity with my countrymen sititha kuganiza bwino

ndele
ndele
5 years ago

ee anafiiila conci mai Mcheka????????????????? koma nde kaloti tu. zimandisekesa ndikakumana ndi azathu ena posawazindikila cifukwa coti anacotsa khungu lacibadwidwe nkulisandutsa la cizungu. sole bola abambo kapena amai ao akanakwatila ndi m china olo azungu. kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

zikomo
zikomo
5 years ago

God will punish this lady in the name of Mcheka chilenje because she has been the one behind the passing of DPP notorious bill in parliamentā€¦..do not cry mcheka time has come for you to be rewarded.uzimuona Kaliati pano akuti akazalowa mu boma ndi Chilima azapanga Bungwe la ACB kuyima palokha koma pa nthawi imene a MCP olikonda ziko la Malawi atalowesa motion imeneyi iye kaliati ndi azake achina Masangwi anavota nawo kuti ‘NO’.

pathfinder
pathfinder
5 years ago
Reply to  zikomo

So zikomo with your stupidity you think that’s a good reason enough for God to punish her? Who are you to decide what God must punish people for? Baasi ukungoona ngati Mulungu ndi choseweretsa chako? Ndi akhristu ngati inu amene anandipangitsa kuti ndisiye kukhulupilira dzipembezo, mumamutenga mulungu kukhala choopsezera anthu. Iwe ngati sunakondwe ndi zosatira za bill sizikutanthauza kuti wenanso sanakondwe wamva. Tsono pokhala Mulungu ndi mlengi okonda ana ake onse sizingatheke kuti atenge kusakondwa kwako kuti alangire nawo wena chikhalirenicho panali wena omwe anakondwa ndi dzosatira za bill.

Namalomba Fredrick
Namalomba Fredrick
5 years ago
Reply to  pathfinder

Inu understanding yazinthu imakuvutani. issue here is that those supporting SKC were part of MPs defeating the independence of ACB motion and now that they are out of DPP they should not stand tall to talk of fighting corruption as ACB which is a corruption watch dog is not independent. So kutukwanaku kukusonyeza umbuli wanu BABA

pathfinder
pathfinder
5 years ago

Chakuti chamako Namalomba werenga bwino lomwe point ya Zikomo, osangotengapo nkhani imodzi iyayi. Kodi ukufuna kundiuza kuti point yomwe ndatsutsana nayo mu comment ya Zikomo ndangoyipeka? Kodi akati God will punish this lady in the name of Mcheka Chilenje akutanthauza chiyani? aaah iwenso pachiphwisi pako ndithu.

Read previous post:
Gerald Phiri to get K11m payout: FA Malawi to hire him for academy project

Football Association of Malawi (FAM) is set to pay Gerald Phiri about K11 million payout after they terminated his services...

Close