Email a copy of '‘Osalubwalubwa’: Sanudi cash-flashing video clip irks Wanderers club' to a friend
Loading ...
Email a copy of '‘Osalubwalubwa’: Sanudi cash-flashing video clip irks Wanderers club' to a friend
Be Forward Wanderers vice captain Alfred Manyozo jnr has said the Nomads have not given up on the CAF Champions...
Bwanji? walakwa chiyani? akunama koma kuti ndi tima change? all the effort these players make in a football pitch, mumawapatsa zingati? zambiri mumatenga inuyo, plus mumakhala nawonso ngongole, mukufuna asamayankhule? this is another era, mmayesa mukuti democracy, eeeee, leave the guys , amamwera zawo. Don’t you know the after effects of drinking beer? you can do anything
Every man has the right to rejoice with his hard earned cash. Palibe nkhani apa. Wamwera zake.
“We are busy looking for assistance from well-wishers”, this is a foolish statement. Mmesa munakana ndalama kwa Sidik Mia. Ndiye mukufuna ma “well wishers” a chani? Does money from a politician smell otherwise?
That”s a personal gesture not representing the whole club why making it a big issue. Just talk to him
Osalubwalubwa big ndi modzi
He is surprised kuti ndalamazo ndi zakedi..it simply shows komwe wakulira.no wonder they think of money first before proving a service to the team.shame.
I’m not surprised, anthu obadwira m’ mapanga, kuona ndalama atamera kale mavuzi
Zopusa izi. Kodi ayamba ndiwowo kukhala ndi ndalama??? Chonchi akufuna Kwa bwino angakalowe Ku Bingu pofuna kuthandiza???? Anayambira popita Ku DRC kulankhula zokhutazo koma management never banything. This one together with his captain need to be discplined.
Sizinakhale bwino