Email a copy of 'Paramount Ngolongoliwa says he is not the UTM architect' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

17 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
mwayamba kale bodza
5 years ago

Leronso mwadaba ya DPP communication master plan yomwe muli fast rail trains. Anthu mungotsatira cha mutu kumadekha.. Kwainuyo ili ndi bodza lankukhuniza chifukwa simungadzakwanitse. I’ve mbava toto,… Aaye…nanga Mr cashgatewo amafunako chainkunsanjako?

mfundoless party
5 years ago

A UTM kambani mfundo musachite chiwewe pomaopseza anthu. Tikufuna atsogoleri opitisa Malawi chitsogolo osati kungokakamira mfundo yoti wakalamba…eeeh uyu mnyamata zero. Ngolongoliwa waphwitsa what’s that. Trush!!. Mutiuze zomwe mudzapange kuposera pa zerodefisiti yomwe anzanu akatakwe akupanga. Chitsankho tiyendetsa tonkha ndi ndalama zathu zamisonkho uwu ndiye ukatakwe nanga inu mudzatani kuposera APA!!!???!

linda apite
5 years ago

A UTM kambani mfundo musachite misala pomakokera mafumu Ku mbali yanu. Ndipo lindani madzi apite ndiye mudzizati tadala. Mfundo zZANU zonse mzodaba KuDPP kupatula ya quota system yomwenso munadaba kwa masiteni(miss cashgate). Komanso Za DPP vutolo zinalitsotha powonjezezera intake komanso kumanga state of art buildings kuonjezera makalasi. Ndiye pali mzeru kuthesa quota system. Ngati milumuzana yonse kuyambira Kamuzu inapanga endorse quota system inu ndi ndani kukaichotsa. Komanso kwa nkhumba mfumu sinkadziwika anthu anali kalikiliki kumenyanirani.

Phwisa
Phwisa
5 years ago

Ngolongoliwa hates Peter despite Peter regarding him as his uncle

Mchape
5 years ago

Wavomela galu ngolongoliwa

Ntengo wa Kesia
Ntengo wa Kesia
5 years ago

APM should have left the mamwene – Paramount – status with the Mkhumbas of Phalombe. The aLhomwe were not really consulted, and were, in the main, against Ngolongoliwa becoming the mamwene. For one thing, there was not a good reason to install the title on this Johnny-come-lately. It was as if APM just wanted to bring the chieftainship near home, to Goliati. But, rather than heed advice, APM went ahead anyway, and made the big mistake of stripping Mkhumba the mamwene status, for the flimsy rationale that the paramount chieftainship should be rotating among the aLhomwe. A procedure unheard of… Read more »

Louis Gobede
Louis Gobede
5 years ago

Zauchitsuru

Yamikani Chirwa
Yamikani Chirwa
5 years ago

DPP ikakuza UTM ikawina tisakumve ukusinthanso zomwe wanenazi. Mbuzi ya munthu mxiiew

The Patriot
The Patriot
5 years ago

From group Village headman to paramount chief in less than 7 years! What a meteoric rise, Mwene wa Mwene tsopano.Inu kudwala mumapita ku India, akamuna tsopano!!! But as they say: chouluka chili chonse chimadzatela. Osazadandaula boma likadzasintha. Ma gulupu enanso zikadzawayendela . Apo ayi sinthani Baba, siyani ndale. Leave politics to politicians Right Honourabl, Professor, Paramount of Paramount Chiefs Ngongoliwa.

Central
Central
5 years ago

Chilichonse choyamba mwa chisawawa chimathanso mwa chisawawa………………………………….! M’dalayu akuoneka wadziwa kuti he is now being pushed to a tight corner and being reduced to his normal size!! Kupupulumamamamamam sikwabwinoooooooooooooo!!

Read previous post:
Mia says real change can come with MCP ‘not the same vultures’

Malawi Congress Party (MCP) vice president Alhadji Muhammad Sidik Mia was on a whistle stop tour in the lakeshore districts...

Close