Email a copy of 'Regime thugs attack Catholic nuns in Lilongwe' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

33 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Operation Nchotsa Mbavas
Operation Nchotsa Mbavas
5 years ago

What the hell is peter doing about these thugs. He has totally lost the plot. How ignorant can one be to the extent of now insulting and harrassing church people and nuns. This is utterly ridiculous. What next we wonder. If we do not do anything about these idiotic barbarians then they will ride all over people even raping women. And the stupid DPP police are just going to look into it. What a bloody joke. These thugs need to be dealt by the mob once and for all. Come on people how can you all tolerate this kind on… Read more »

Nzika ya Malawi
Nzika ya Malawi
5 years ago

Namalamba ukunena zoona osati chitsiru chikudzitchula kuti Vision’cho. Ndani amadzola paint ya blue m’dziko muno oposa ma cadet? Afisi amenewa atikwana!

Nzika ya Malawi
Nzika ya Malawi
5 years ago

Koma Dausi ndiwe mfiti yodya maliro ndithu! Chithunzicho chikuonetsa ndani galu iwe? Umathandizana ndi mkazi wako Wa Jeffrey kumawapatsa achombwewo ndalama kuti azipha anthu ngati momwe umachitira nthawi ya Kamuzu. Mulungu akukantheni nonse afisi a DPP ndi Ibu yemwe

Achiswe
5 years ago

If the DPP is not behind these attacks on opposition targets, why does it not instruct the police to investigate them to find out who is really responsible for them. Merely condemning them is not enough; action is needed if we are to believe that the DPP has no involvement. Until such action is taken by the forces of law and order to discover the real culprits and to prosecute them, there is no alternative but to lay the blame at the door of the DPP.

Achiswe
5 years ago

The DPP is no longer the DEMOCRATIC People’s Party; it should now change its name to the CPP – the CORRUPT People’s Party. It has reverted to the bad old days of Kamuzu Banda with his MYP and Youth Leagues. By adopting these former MCP tactics the ruling party is making itself unelectable. It has ceased to be a People’s Party as the people long since rejected such terror tactics.

chimanga Chaponda
5 years ago

Kadauluka kadzatela….. DPP and your Police Chiefs will one day pay for this

Kibaki
Kibaki
5 years ago

end of DPP

Hard Truth
Hard Truth
5 years ago
Reply to  Kibaki

Munayamba kalekale kuyimba nyimbo imeneyi. When exactly the mighty DPP is going to end? You will here again tomorrow singing the same song, “end of DPP”. Hahahaha let 2019 come and we will shame you.

Vision
Vision
5 years ago

Komatu a Malawi tisamangokhulupilira zili zonse. Zinthuzi zilibe umboni. Panopa aliyense angoti DPP. China chilichonse DPP. Kodi a Malawi sitingathe kuganiza kuti enanso angotengerapo mwayi popeza aliyense angoti DPP. Anthu akhozanso kumangobisalira ku DPP ali anthu wotumizidwa ndi UTM. *Musayiwale ku Mangochi adadziwotchera magalimoto kufuna sympathy*. *A Mtambo adadziwotchera office kufuna kuti ma Donor awamvere awapatse ndalama chifukwa amadziwa kuti anthu atopa nawo ndipo kumseu ko sakapitako*. Lero akutuma anyamata kuti avare zovala za DPP kukamenya ma Nun cholinga anthu awa khulupilire. Don’t you people see that anthuwa akuti sewera heavy. Kufuna ma udindo, kusaka ndalama kwavuta pa Malawi. Uyuyu… Read more »

Namalomba Fredrick
Namalomba Fredrick
5 years ago
Reply to  Vision

Iwe mutu wako sugwira ntchito, akanakhala kuti si a DPP bwenzi atagwidwa, these are moves spearheaded by DPP machinery. PERIOD

pathfinder
pathfinder
5 years ago

Aise Namalomba ndikukumvesetsa kumbali yako, komano ndikanakondanso ukanamumvesetsa Vision usanamutukwane. Pachithunzi chomwe achita post a nyasatime makamaka bambo chiuta, mukuonapo minbus yomwe yanyamula anamwino a katolika? nanga masapota a dpp ali pamenepo mukuwaona atanyamula ndodo zomenyera anthu? Komanso mukaona chithunzicho, sichikufanana ndi chithunzi chomwe anaposita a nyasatimes pa nkhani yoti ma cadet anabvutitsa mayi kaliat ku parliament? Mukadzifunsa mafunso awa ndikupeza mayankho muchilungamo mosawerengela ndi kudana kwanu ndi chipani cha DPP mukhoza kukhala ndi ufulu wa mumtima.

Mchacha the Terrorist
Mchacha the Terrorist
5 years ago
Reply to  pathfinder

@ pathfinder
Why should we waste time calculating 1+1 using calculus or pythagolus when we simply know that 1+1 answer is 2. We are not chicken brain as you are pathfinder to be applying the principles and ideals of calculus or pythogolus to calculate 1+1. We have for long talked about this unbecoming behavour of DPP cadets under the tutulege of mchacha but your inept and clueless mutharika can’t rein over them. No pathfinder don’t take Malawians for fools. It’s simply stupid to do that. Write again chicken brain

LEGO
5 years ago
Reply to  Vision

STUPID,IDIOT

Bob
Bob
5 years ago

Is this democracy or war against fellow Malawians? If you fail to lead your members politically don’t take the masses for granted.

ndele
ndele
5 years ago

MBUTUMA IZI NDI MBUYANU YEMWE .SALUDZIWA TAWAJAMBULA. MANYIII ANU KUNUNKHA VIFWENTHE ETI

Read previous post:
SKC pledges to develop sports from grassroots level

State Vice President Dr. Saulos Klaus Chilima, who is fondly called SKC,  has pledged to develop sports from grassroots level...

Close