Sulumba unveiled at Nyasa Bullets: Malawi champs start training
TNM Super League champions Nyasa Big Bullets have unveiled their new signing Muhamad Sulumba from Blantyre United after signing a three-year contract, frustrating Mighty Be Forward Wanderers who wanted to sign him for permanent after a successful loan stint last season.
Bullets chairman Samuel Chilunga hailed Sulumba “one of the top strikers in Malawi.”
Chilunga was delighted that the striker had agreed to join the ranks at the Peoples Team after making a dramatic U-turn over his move to Lali Lubani Road – the home of Wanderers.
Sulumba said he was attracted by the character of Bullets and their reputation for never giving up, even claiming they were going to defend the Super League title for the third year.
“What I like the most about Bullets is the character. It’s a new challenge for me. Excited to be at my new home Bullets,” said Sulumba.
According to Chilunga the People’s Team resumed training on Tuesday at Kamuzu Stadium under the guidance of Mabvuto Lungu and Lloyd Nkhwazi.
Lungu will not going to guide the team to the title defence because who does not hold a CAF B license which the Football Association of Malawi (FAM)—under the Club Licensing System (CLS)—is enforcing as a minimum requirement for the top-flight league coaches.
Bullets former centre back George Nyirenda has also resumed training with the club after terminating his contract with top Zimbabwean side Caps United.
The club has also two realists from Southern Region Football Association (SRFA) Premier League side Ndirande Icons.
Welcome to the people’s team chisankho chabwino uncle sulumba takunyadilani winayo zimuwawe basi
a sulumba mwationjezatu apa ife anyerere ayi mwakhwana ndiinu .anyway zabwino zonse tionana zikayambika .
neba usayike 100% pa sulumba ukhumudwa usaiwale kut ma player akumalawi amatchuka season imodzi ndiye uziwona.
palibe vuto apa dzina loti SULUMBA yapanga ndi NOMA anali ndani ali ku BT UNITED?
Wabwino sasowa, tiyenazo neba. Mwina akupindulira iweyo. Wishng u all the best Neba.
abutawo asamatiyese ife a noma bwanji mumatinamiza kt surumba ndi wathu ife anoma zopusazo ayi uzikanamiza akazako
abutawo osamatinamiza ife c ana mwava atirandaso sulumba mesa mumati ndi wathu ife anoma aaa zopusa bas
sulumba ndi gold koma anoma zinawavuta kumgwiritsa kwake ntchito odziwa kumkhalitsa kukhala osadziwa mpira neba ati adzakupweteke ndiyemweyu tsiku lokumanalo.
BANJA LIKATHA OSAMATI MKAZIYU SAMADZIWA NTCHITO ZAKUCHIPINDA,CHIFUKWA CHENECHENE WACHOKELA MWANAYU MULUCHIDZIWA,KOMA KUSAFUNA UVOMELAZA,NIMASEWERO YAWA SIZAKUDAMBWE MILANDU PALIPONSE.YAWA INE;AHH!YEKWE
wagwa nayo neba sulumba ndi dili osati wadabwa kkkkkk
kkkkk usova wa noma kwa ife ndi dilu basi ala.
Sulumba agwirantchito season ino
I thought Nyasa Bullets are on a two weeks ban by FAM not to conduct any football business in this country due to failure to comply with club lincensing requirements? I stand to be corrected.
Osati bwetubwetu mmmmh sibwino nanga ichi nchiani chachitika ………. Kani anthua akulu amanamanso eti…… Mr Rashy kkkkkkkkkkkkkkkkkk
zachiphuliphuli kuzanso wa mmakwalala ndi noma sizigwirizana…big up nyerere for grabbing young lads like tambe who can play skilful soccer.
thanks NYASA,thanks CHILUNGA..That is we call coming .chaka chino si chonyengelera big names should be playing big club.bring more aziwanso ma neighbor wo.
Rashy ukuti bwanji tsano? Sunayambe kutsegula m’mimba?kikikikikikiki…..tinakuuzani pakamwa sipasewela mpira tsano ndizimenezi’tu. Ineyo monga wa Nyerere sindine odabwa kuchoka kwa Sulumba. Ma player athu sitikuwasamala kuno ku Noma ndipo ndi ambiri omwe akuchoka. Koma Sulumba nde atinyetsatu season ikubwerayi ndipo tiziona…
Kunena kwa ndithendithe Gaffar Rashid wagwira anko chiphwisi,kkkkkkkk pyandikomera maningi mbuya.
Ngati SULUMBA watha kale inuyo mumamufunilanji? Mkamkhazika pa bench ndinuyo.
Khalani phee Sulumba. Ndi Mlengi yokha adziwa tsogolo lanu. By the way incentives determine one work output. Who knows perhaps there are more inicetives at Nyasa Bullets than some other clubs such as yours.
he is finally ours a good development
Sulumba alibe ntchito tidatenga carlsberg kulibe sulumbu iye bb sakuyidziwa kuphonya kuja amaphonya timuyake si bb ukathera pa bench uzaifuna noma. Ku frames sakukutenga udatha.
Tsoka